Malawi Voice TV & FM

Malawi Voice TV & FM

Compartir

Content Creator/Daily News/Daily MEMES
‼️PLEASE FOLLOW ME FOR MORE ‼️‼️
🚩EVERY NEWS ACROSS MALAWI🚩

04/09/2026

GABA WAKANA ZOTI ANAWINJA MWANA WA FORMER FLAMES COACH, PATRICK MABEDI — ANITA MABEDI

—Kwa miyezi ingapo, pa social media pakhala pali mkangano komanso mphekesela zak*ti wosewela mpira Gaba Mhango amawinjana ndi Madam Football (Anita Mabedi), mwana wamkazi wa mphunzitsi wakale wa Flames, Patrick Mabedi. Nkhaniyi inadzetsa debate kwambiri pa social media, pomwe anthu ambiri ankafunsa k*ti, “Kodi zoona zake ndi ziti?”

Koma dzulo, Gaba anafotokoza mbali yake ya nkhaniyi ndipo anakana kwa mutu wagalu k*ti sanamupakulepo Anita Mabedi. Iye anapitiliza kufotokoza k*ti munthu yemwe anali naye (kuzemberana) anali m’nzake wa Anita, osati Anita mwiniwake.

Komabe, Gaba anavomeleza k*ti sinali AI ,iyeyo ndi Anita anali pamodzi ndi anthu ena ankangocheza m’nyumba ndikumajambula ma clip apa TikTok, ndipo kenako anapsopsonanadi. Anamupatsa kiss yomwe iye anati anali “French kiss.”

Pakadali pano Anita akumamuyitana GABA k*ti Bro ndicholinga choti anthu mukhulupilire Kuti anthuwa sanakhalepo pachibwenzi olo ndi tsiku limodzi sadapangepo zausatana limodzi.

Photos from Malawi Voice TV & FM's post 04/09/2026

⚽🇲🇼Mbiri ya kochokera Kwa Gabadinho Mhango 🇲🇼

Gabadinho Mhango, yemwe dzina lake lonse ndi Hellings Frank Mhango, anabadwa pa 27 September 1992 ku Chiweta, Malawi.

Iye anakulira m’banja lomwe linali ndi moyo wovuta, ndipo makolo ake ankavutika kupeza zofunika pa moyo. Ngakhale makolo ake anali osagwira ntchito panthawiyo.

Ali mwana, Gaba ankakonda kwambiri mpira. Ankasewera ndi anzake pogwiritsa ntchito mipira yopangidwa ndi mapepala apulasitiki, komanso ankathera nthawi akusodza m’dera la Chiweta. Izi zikusonyeza k*ti luso lake la mpira linayambira ali mwana, asanakhale katswiri.

Ngakhale moyo wa m’banja sunali wophweka, Gaba sanaleke kulota za kukhala katswiri wa mpira. Makolo ake ankafuna k*ti apitirize sukulu, ndipo iye anafika posankha kuika mphamvu zambiri pa mpira. M’kupita kwa nthawi, luso lake linamuthandiza kuchoka ku Chiweta kupita ku Brave Warriors, kenako Big Bullets, ndipo pambuyo pake anayamba kusewera ku South Africa.

Taonani Pamene Ali Gabadinho Mhango PANO!! ili ndi phunziro Kwa inunsoo
mpasen like wake basiii🇲🇼

04/09/2026

Osewela wa ku Zambia Fashion Sakala yemwe amasewela League yaku Saudi Arabia akupitilila kuchita bwino pamene wapambana Mphotho ya Man of the match ulendo ungapo otsogoza.

Dzulo Sakala anagoletsa chigoli chimodzi ndikusakhidwa kukhala Man of the match pamasewelo omwe timu yake ya AI Fayha yalephelana 2-2 ndi AI Kholood.

Miyezi yapitayo Sakala anathandiza Mayi wina ovutika kuno ku Malawi ndi Ndalama zokwana K1.3 Million kudzela mwa Rodwell Lumbe yemwe amagwila tchito za Chifundo.

04/09/2026

FAM Yachenjeza Matimu Kuti Asamachotse Osewera Mochedwa

Pamene Msika ogula komaso kugulitsa wayamba Bungwe la Football Association of Malawi (FAM) lachenjeza matimu k*ti asamachotse kapena kupanga realese osewera omwe sakuwafuna mochedwa pongwe nthawi imakhala k*t yatha kale

FAM yati mchitidwewu umapatsa osewera mavuto, chifukwa amatha kusowa nthawi yokwanira yopeza timu yatsopano.

Msika wa 2026/27 unatsegulidwa week yatha ndipo ukuyembekezeka k*tsekedwa pa September 21.

Note : chinthuzipo yangoikapo
📸 Blantyre Broadcasting

04/09/2026

🚨WANDERERS SET TO PART WAYS WITH PROLIFIC FORWARD KUMWEMBE🚨

The Match Assessor has gathered the information that, Mighty Wanderers Football Club has started to rule out the idea of re-signing their deadly forward Christopher Kumwembe, who came to the country from Zambia where he was playing on loan.

An investigation by The Match Assessor on Friday morning found that since arriving in the country, Kumwembe has not reported for training with the Nomads.

According to an inside source, club officials say they even do not know where the player is staying and have not entered into any contract negotiations with him.

"Kumwembe sakuwoneka ndipo sanapedzekepo ku Training nditimuyi chibwelereni akungozemba, komabe tikamupedza timumva bwino maganizo ake" The Source said.

The Match Assessor understands that Kumwembe is demanding a large sum of money to stay at the club after arriving from Zambia. Amid the standoff, rumours have circulated that he is instead pushing for a move to FCB Nyasa Big Bullets.

In team news, Wanderers will also be without dependable defender Alex Kambilinya for Sunday’s match due to injury.

The Nomads are currently in Lilongwe preparing for their CAF Confederation Cup fixture against Simba SC on Sunday.

Photos from Malawi Voice TV & FM's post 04/09/2026

✈️🇹🇿 SIMBA SC YANYAMUKA

Simba SC yanyamuka ku Julius Nyerere International Airport ku Dar es Salaam, Tanzania, pomwe ikubwela kuno Ku Malawi kukakumana ndi Mighty Wanderers mu CAF Champions League.

🏆 CAF Champions League
⚔️ Mighty Wanderers 🆚 Simba SC
📅 Sunday , 6 September
🏟️ Bingu National Stadium

Nde paja Amavala zofiika Kaya saphwetekeledwa za eni ake Kaya asimbawa koma akundimvetsa chisoni

follow Malawi Voice TV & FM

04/09/2026

📌⚽️♨️Goloboyi Number 1 Kutimu ya Silver Strikers George Chikooka akukana kusaina contract yatsopano timuyi itamupempha k*ti awonjezere mgwirizano wawo.

Sports Battalion Malawi yapeze k*ti Chikooka wafikilidwa ndi matimu aku Zimbambwe ndipo iye wapanga chiganizo cholowera mdziko la Zimbambwe.

04/09/2026

Pamene dziko lonse likukumbukira Mwezi wa Kuzindikira za Kudzipha mwezi wa September, akatswiri a zaumoyo apempha boma komanso adindo osiyanasiyana k*ti ayike njira zatsopano zomwe zithandizire kupewa nchitidwewu.

Polankhula ndi Jojo FM, Thokozire Kadango, katswiri wa zaumoyo wati ngakhale zokambirana zokhudza malingaliro angwiro zilipo pali zina zambiri zomwe zikufunikabe kuchitidwa.

Kadango wati boma ndi mabungwe akuyenera kuchulukitsa mauthenga a kuopsya kodzipha m’masukulu ndi zipatala, kupereka maphunziro kwa aphunzitsi ndi atsogoleri achipembedzo, komanso kukhazikitsa mapulogalamu ammudzi omwe angathandize anthu .

Iye anawonjezera k*ti achinyamata ndi abambo ndi omwe akukhudzidwa kwambiri ndi vuto la kudzipha m’dziko muno.
.

Photos from Malawi Voice TV & FM's post 04/09/2026

Timu yochita masewero osambira yayamba bwino ku mpikisano wa 2026 Africa Aquatics Zone IV ku Gaborone m'dziko la Botswana, pamene Tasunge Mkavea komanso Davina Chongwe apeza mendulo za bronze pa tsiku loyamba la mpikisanowu.

Mkavea wapeza mendulo atapikisana mu gawo la osambira anyamata a zaka 15-16 pa mtunda wa 50 mitres, pamene Chongwe yemwe ndi mtsikana wa zaka 12 analandira mendulo ya bronze atathera panambala yachitatu pa mtunda wa 800 mitres.

Mpikisanowu udzatha loweruka pa 5 September 2026.

04/09/2026



Maranatha Academy has commended its former student, Ireen Navicha, for representing Malawi at the Miss World competition, describing her performance as a reflection of the values of discipline, excellence and service promoted by the institution.

In a statement, the academy said it is particularly proud of Navicha’s achievement in reaching the Top 24 in the Beauty With a Purpose category, which recognises contestants who use their platforms to promote initiatives that benefit communities.

By McDonald Chiwayula

https://mbc.mw/maranatha-academy-to-honour-miss-world-contestant/

¿Quieres que tu empresa sea el Gimnasio mas cotizado en Madrid?

Haga clic aquí para reclamar su Entrada Patrocinada.

Localización

Página web

Dirección

Post Office Box 28
Madrid