Business plug

Business plug

Share

Let's talk about football

02/09/2025

Katswiri wa Chelsea walowela ku bayern Munich pa ngongole

02/09/2025

Katswiri wa mmbali wa man United walowela ku aston villa pa ngongole

02/09/2025

Kuchoka ku abwenzi pano ndi adani pa mpira anali banja limodz pano anatenga njira zosiyana

Anyway congrats wissa ku team yako yatsopano Newcastle United

19/08/2025

Team ya leeds yapambadza team ya Everton usiku wa dzulo

Leeds 1-0Everton

Mmenemu ndimene zayendela dzulo

18/08/2025

Nkhani yomwe yachema ku England

Yoane Wissa wapanga unfollow Brentford,ndipo wasintha profile picture to black and wachotsa ma photos ake onse pa instagram account yake pamene akuoneka ngati akufuna kuchoka ku club imeneyi.

18/08/2025

Zinali motele dzulo ku England 👇👇

Manchester United yagonja pakhomo ndi team ija ya arsenal
United 0-1arsenal

Team ya Chelsea yafananitsa mphamvu ndi timu ya Crystal palace atalephelana kuchinyana
Chelsea 0-0crystal palace

Team ya Nottingham yagagada team ya Brentford

Nottingham 3-1Brentford

Menemu ndimene zayendela dzulo ku England

16/08/2025
16/08/2025



Lero pa 16 August umu ndi mene zayendela ku mangalande

Wolves yagonja pakhomo ndi time ya Manchester city ku zigoli 4 kwa 0

Thomas frank zake zayamba bwino ndithu pamene timu yake ya Tottenham yapeza chipambano pogonjetsa burnley ndi zigoli 3 kwa o

Anyamata a Newcastle zawo sizinawayendele pamene afananitsa mphamvu ndi timu ya aston villa ngakhale aston villa inali ndi red card palibe amene anawona pa golo pa mdzake pamene masewela atela 0 kwa 0


West ham United yagonja ndi timu ya Sunderland yomwe yalowa kuchoka ku championship ndi zigoli 3 kwa 0

Brighton yafananitsa mphamvu ndi timu ya Fulham ndi zigoli 1 kwa 1

Mmenemo ndimene zayendela ku England
Ndipo mkhondo ilipo lipo mawa pamene arsenal ikukumana ndi Manchester United

Gyokeres vs sesko

16/08/2025

Bournemouth machine adha awawa amaika effort pangolin wawa ndiamene ali a top score padakali pano

🚨 Premier League Top scorers! 🏴󠁧󠁢󠁥󠁮󠁧󠁿✨

1️⃣ 🇬🇭 Antoine Semenyo – ⚽⚽ (2 Goals)
2️⃣ 🇫🇷 Hugo Ekitike – ⚽ (1 Goal)
3️⃣ 🇳🇱 Cody Gakpo – ⚽ (1 Goal)
4️⃣ 🇮🇹 Federico Chiesa – ⚽ (1 Goal)
5️⃣ 🇪🇬 Mohamed Salah – ⚽ (1 Goal)

16/08/2025

✅⚽️ chigoli chake choyamba mu Premier league.
✅🅰️ Assist yake yoyamba muPremier League .
✅🏆 Award yake yoyamba mu premier league

Pangolin wa liverpool Hugo Ekitike. 🔴

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Blantyre?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Website

Address

Blantyre