NEXT GAME 🎮
FCB NYASA BIG BULLETS 🆚️ BLUE EAGLES
KAMUZU STADIUM 🏟/27JULY25
PREDICTION YANU IKUTI BWANJI MAULE MWAMATAMA
# FCB nyasa big bullets news
Fcb Nyasa big bullets news
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Fcb Nyasa big bullets news, Sports League, Blantyre.
Maule amene akufuna WhatsApp group la fcb Nyasa Big Bullets 0995600171 changu Maule tikupangeni add now🔥🔥🔥🇦🇹🇦🇹
# fcb nyasa big bullets
Tikupang after 1 week
10/07/2025
What a fixture next week
🤣🔥🔥🔥
Maule mwanayo mwanayo
02/07/2025
EKHAYA FC 🆚️ FCB NYASA BIG BULLETS
KAMUZU STADIUM 🏟
KICK OFF 14:30😊
Ife takozeka kugonjesa Ekhaya FC lero pa Kamuzu Stadium.....Mike Mkwate, Babatunde Adepoju, Peter Banda, Chawanangwa Gumbo, Thengo, Petro, Chikumbutso Salima, Hassan Kajoke, Loyd Aaron, Yamikan Mologeni, Henery Chiwaya, Andrew Jovinala ndi alimbikisa masapoto tonse kuti bwerani muzaipase moto lero pa Kamuzu Stadium 🏟.
ngati uli sapota wa FCB Nyasa Big Bullets tangolemba Prediction yako apa kuti neighbor azipsa mtima Ndimasapota a Ekhaya FC
# FCB Nyasa big bullets news
02/07/2025
Mwati apa sapwetekana awa🤣🤣
Ndiy wamuona wangayo chomwe wabisacho ndi babatunde ameney mwina winawe sukudziwa
26/06/2025
NKHANI YABWINO KU MAPALE ONSE 🇦🇹🇦🇹🇦🇹
Osewera wa pakati mu timu ya FCB Nyasa Big Bullets, Yankho Singo, akunyamuka mdziko muno loweruka likudzali, pa 27 June, 2025 kupita ku South Africa kumene akukayamba kusewera mu timu ya Lamontville Golden Arrows imene imasewera mu ligi yayikulu mdzikolo, ya BetWay Premiership.
Singo yemwe ali ndi zaka 24, sanasewere masewero atatu amene Bullets yasewera ndi timu ya Mighty Tigers komanso Moyale Barracks mu ligi ya TNM.
Iye sanapezekenso pamasewero omwe Bullets imasewera ndi Karonga United mu chikho cha Airtel Top 8.
Malinga ndi kafukufuku wathu, Lamontville Golden Arrows yagula Singo pa mtengo wa 75 million Kwacha ndipo akuyembekezeka kusayina contract ya zaka ziwiri.
Koma mkulu oyendetsa ntchito za timu ya FCB Nyasa Big Bullets a Albert Chigoga wati Yankho Singo sakusewera kaamba koti ndi ovulala ndipo si zoona zoti akuchoka komabe a Chigoga ati sangamuletse osewerayu patakhala matimu ena a kunja omwe angamufune.
Zimayamba ndi Mapale 🇦🇹🇦🇹 🇦🇹 🇦🇹
# FCB Nyasa big bullets news 🖍️
25/06/2025
Job done in style! 🔥
Bullets 3-0 Moyale
(Salima 11’, McBrams 37’, Gumbo 87’)
Big goals, clean sheet, birthday scenes — what an afternoon at Kamuzu! 🎯🎂🔴
# FCB Nyasa big bullets news
25/06/2025
Happy birthday 🎂🎂🎂🥳 yokoma kwambiri
25/06/2025
Drop your prediction 🇦🇹
25/06/2025
Click here to claim your Sponsored Listing.