Good night angerezi π
See you tomorrow at Mpira Stadium π
Mighty wanderers fc fans
Welcome to the mighty wanderers fans page keep up to follow this page ππππππ π΅π΅π΅π΅π΅π΅βͺ
Tikumbusanepo apa zamawa
Wanderers vs Red Lions
Mpira stadium ποΈ 2:30
Mighty wanderers vs Ekhaya FC 30 08. 2026 final top 8
Bingu stadium π 14:30
21/08/2026
Inu tipaseni chinthucho kuno nkholo sangavute kukwapula mwana wake please tipaseni tichisungiletu IFE kuno
Inu team ndiyomweyi inu mukuchedwa kuti ngat iweyo uli sapota wa wanderers sungaduse osapanga like komaso follow page ino angerezi please
21/08/2026
πKod inu amalawi mupole moto mwava kod Malawi π²πΌ muno alimo mkazi ekha. Uyu mwakonda chifukwa chani sopano enawa azapana ndani mundisamale mwava. Ndinamuvela kuwawa uyu oho ππ
Ndiwe sapota wa wanderers kuchokera boma lanji tiziwane please angerezi ππ
20/08/2026
ππ Sorry mwina mudayiwala timati tikukumbuseni ππ
NDIKUFUNA MUNTHU MODZI OTI ANKHALE A DIMIN A PAGE INO TIYENI TIKUMANE KU COMMENT SECTION π
20/08/2026
KUMENE ILI RED LIONS KO IKUONA NGATI PA 22 SIPAFIKA π ANA ANYAPIDWA AMENEAJA EYA TIKUZIWA K*T AMAZIWA ZIGOGODO KOMA PA IFEYO SANGADUSE π
Click here to claim your Sponsored Listing.