ChewaSports Zone

ChewaSports Zone From the Super League to the Premier League, we cover it all. Real football talk. Real passion. Made for Fans, By Fans.

Rob Edwards nde mphunzitsi watsopano wa team ya Wolves.Edward wavomera k*tikitira contract ya dzaka zitatu ndi theka. Nd...
10/11/2025

Rob Edwards nde mphunzitsi watsopano wa team ya Wolves.

Edward wavomera k*tikitira contract ya dzaka zitatu ndi theka. Ndipo team ya Middlebrough ilandira ndalamwa zokwana £3M ngati chipuputa msozi.

 Silver Strikers 1 (5) - 1 (4) Mighty WanderersA Malawi lero ayikira umboni pa masewero omwe anapereka chikoka kwambiri,...
09/11/2025



Silver Strikers 1 (5) - 1 (4) Mighty Wanderers

A Malawi lero ayikira umboni pa masewero omwe anapereka chikoka kwambiri, pamene Silver Strikers yakwanitsa kupambana kudzera pama penote masewerowa atathera 1-1 mu mphindi 90 komaso zisanu zoonjezera.

Dalitso Nkhungwa anayesesa kumbali kuchosa mapenote angapo onse k*ti mwina team yake ingatengeko koyamba chikho cha FDH bank Cup.

Koma naye George Chikooka anakaniza golo lake mapenote a Wanderers k*ti atenge chikho pa mutu pake.

Nickson Mwase ndi amene wachita kuweruka k*ti akwanitse kupambana chikho cha FDH kawiri tsopano.

Otsatira team ya Wanderers akuyang'anirabe k*ti ndi liti azatenge chikho chomwe oyitsatira ena amachitcha cha mbuyawo.

 Tottenham Hotspur 2-2 Manchester United. Richarlison thought he scored the winning goal the moment after Matthijs de Li...
08/11/2025



Tottenham Hotspur 2-2 Manchester United.

Richarlison thought he scored the winning goal the moment after Matthijs de Ligt heads the ball into Spurs net through a corner kick.

Mphunzitsi wa Malawi National Team Kalisto Pasuwa watulutsa ndandanda wa anyamata okwanira 26 k*ti akasewere nawo masewe...
08/11/2025

Mphunzitsi wa Malawi National Team Kalisto Pasuwa watulutsa ndandanda wa anyamata okwanira 26 k*ti akasewere nawo masewero apa ubale ndi team ya Lesotho.

FLAMES SQUAD
FOR FRIENDLY MATCHES AGAINST LESOTHO

GOALKEEPERS
William Thole (Simba Bhora)
George Chikooka (Silver Strikers)
Joshua Waka (Ekhaya Fc)

DEFENDERS
Nickson Nyasulu (FC Platinum)
Emmanuel Nyirenda (Mighty Wanderers)
Maxwell Paipi (Silver Strikers)
Alick Lungu (Ekhaya FC)
Blessings Mpokera (FCB Nyasa Big Bullets)
Mcdonald Lameck (Silver Strikers)
Jubril Okedina (Bohemiens)
Charles Petro (FC Botosani)

MIDFIELDERS
Yankho Singo (FCB Nyasa Big Bullets)
Blessings Singini (Mighty Wanderers FC)
Lloyd Aaron (Muaither SC)
Lloyd Njaliwa (Costa Do Sol)
Robert Saizi (Zanaco)
Uchizi Vunga (Silver Strikers)

FORWARDS
Patrick Mwaungulu (TP Mazembe)
Chikumbutso Salima (FCB Nyasa Big Bullets)
Lanjesi Nkhoma (TP Mazembe)
Mayele Malango (Monterey Bay FC)
Gabadinho Mhango (Richards Bay)
Chifundo Mphasi (Power Dynamos)
Babatunde Adepoju (FCB Nyasa Big Bullets)
Andrew Joseph (Silver Strikers)
Yann Kouakou (Europa Point FC)

Team ya Middlesbrough yapanga chiganizo choyimitsa kaye ntchito mphunzitsi wawo Rob Edwards k*ti lero asakhale nawo pa t...
08/11/2025

Team ya Middlesbrough yapanga chiganizo choyimitsa kaye ntchito mphunzitsi wawo Rob Edwards k*ti lero asakhale nawo pa touchline pamene team yawo ikukumana ndi Birmingham City.

Rob Edwards akufunidwa ndi team ya Wolves k*ti akakhale mphunzitsi wawo ndipo team ya Middlesbrough yakhala ikumukaniza Rob Edwards, koma iye mwini zikuwonetsa ngati akufuna atapita ndikukaphunzitsa team ya Wolves mu Premier League.

Pa chifukwa chimenechi Middlebrough yapanga chiganizo k*ti Rob Edwards asakhale pa touchline ndikumayiwuza team yake zoyenera zochita. Kuopa k*ti patha kukhala ziwiri zitatu zosokoneza.

Osewera wa Manchester United. Kobbie Mainoo wasiyidwa mu squad yomwe yalowera ku London komwe akukawonetsana chamuna ndi...
07/11/2025

Osewera wa Manchester United. Kobbie Mainoo wasiyidwa mu squad yomwe yalowera ku London komwe akukawonetsana chamuna ndi team ya Tottenham Hotspur.

Pa masewero 4 omwe ma team'wa asewera mbuyo, Manchester United sinakwanitse kupeza chipambano chilichonse pamwamba pa team ya Spurs ndipo sanakwanitse kupezako olo point imodzi.

Mphunzitsi wa Manchester United watenga osewera wachisodzera Jack Fletcher amene bambo ake anaseweleraso Manchester United dzaka zingapo zapitazo.

Atakhala pafupi pafupi asanapambane masewero awiri otsogozana. Ruben Amorim ndi anyamata ake mwezi wa October anawonetsa...
07/11/2025

Atakhala pafupi pafupi asanapambane masewero awiri otsogozana. Ruben Amorim ndi anyamata ake mwezi wa October anawonetsa chamuna pamene anakwanitsa kupambana masewero onse atatu omwe anali mweziwu.

Manchester United inapambadza team ya Sunderland pankhomo ndi zigoli ziwiri kwa chilowere.

Pa 19 October anakwanitsa kuwonetsa chakuda Liverpool pakwawo, pomwe akhala ak*tamika k*ti anzawowa sanawamenyepo kwa dzaka 10. Masewerowa anathera 1-2

Manchester United sinathere pomwepo. Anayitana team ya Brighton Hove & Albion pomwe anakwanitsa kuyichita chipongwe ndi zigoli zinayi kwa ziwiri.

Zotsatirazi zapangitsa k*ti Ruben Amorim apambane mphoto ya mphunzitsi amene wachita bwino mweziwu. Komaso Bryan Mbeumo wakhala osewera amene wachita bwino mwezi wa January.

07/11/2025

Osewera wa team ya Arsenal Gabriel Jesus yemwe wakhara ali ku Injury Kwa thawi yayitari dzulo wabwerera ku ma training ake ndipo akuyembekezera k*t atha kusewera nawo masewero omwe akubwerawa

Ma game aku Carabao Quarter Final akungidwa
06/11/2025

Ma game aku Carabao Quarter Final akungidwa

06/11/2025

🚨🚨| Ma team a Liverpool komaso Manchester United. Akhala ak*tsatira nyamata wina yemwe amasewera team ya Hertha Berlin waku Germany, Kennet Eichhorn.

Hertha Berlin yati ifunapo ndalama zokwana £17M pa Kennet Eichhorn.

report!!!

[Manchester United-Malawi🇲🇼]

Address

Chilomoni
Chilomoni
312212

Telephone

+265884697656

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when ChewaSports Zone posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to ChewaSports Zone:

Shortcuts

Share

Category