08/12/2024
Chelsea the blues starting player against spurs
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Munlo News Talk-Mwamva Chani"., Sport & recreation, Munlo Trading Centre, Chiradzulu.
08/12/2024
Chelsea the blues starting player against spurs
08/12/2024
Tili kopepha mafuta pano ulendo waku kenani uja tikuyenda chokwawa kuno
06/12/2024
Tilibe kunena zambiri muzonse tingot amen🙏🙏🙏🙏
Kwacha bwanj kumeneko,,, anthu kafunsana k*t kod ulendo waku kenani mukatilonjeza uja ndi umenewu🤔🤔😕😟🥲😭😭
Mwez uno ngat mkaz akukukana uzifunse ndithu 🤣🤣🥺🥺
Boma ndilomweli Ali kwa asilamu kopepha mafuta pano🥺😛🤣🤣🤔
Nde zikhale k*t amagwira ntchto ndi mkaz pakhomopo pena amatha kukuuzatu k*t ukolope🤠😎🤔🤣🤣 ATI iye watopa
Timati mwina Manchester united yauka kma mmmm ayi tidikirebe ndithu🤣🤣🤣
Mkulu wina oziwika ndikukhoma zidebe kmaso mapoto mudzi mwa Masauli wapezeka ndi apongozi ake akazi akugonana, owagwira ndie kukhala apongozi ake amuna
Moyaa tawapatseni moni ma sapota a man city omwe mumacheza nawo🤣🤣
Manzy kausiwa muli makola emwe🤝🤝