Aku Dowa

Aku Dowa

Share

Follow my page I follow you back let's go

Photos from Aku Dowa's post 27/06/2024

Muti zukhala bwanji Kodi πŸ˜‚πŸ˜‚πŸ˜‚ follow and like my page kuli zithuπŸ€”πŸ€”

27/06/2024

Kudutsa pa chikondi kufika pa loveπŸ˜‚πŸ˜‚πŸ€”πŸ€”

27/06/2024

Isaac Jomo Osman

Akuti anakakhala kuti adakali pachiongolero ku timu ya FCB Nyasa Big Bullets anakachotsa osewera onse amene akuyambitsa nkhalidwe onyanyala training komanso kupangitsa kuti timuyi isamachite bwino.

Jomo wati zikufukwa zimene akupereka osewerawa popanga izi ndi zosamveka chifukwa kuli osewera ena kumatimu ena amene akuvutika.

Kusalandira K40,000 ngati zili zoona sizokwanira kupangira izi malingana ndi Jomo.

Akuti kunali osewera ena amene anayivutikira timuyi kuti ifike pomwe ilipa pa nthawi imene inalibe kanthu.

✍️

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Dowa?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Telephone

Website

Address

Dowa