Choyamba, Tidye

Choyamba, Tidye

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Choyamba, Tidye, Mzuzu.

09/03/2026

Kwacha koma choyamba tidye!

Mpunga wa Kilombero, mtengo ndi:
5kg - k30,000
2kg - k12,000

Ufa wa gaiwa, gramil ndi oyera wama vitamins ndima Minerals uliponso.

Mtengo:
5kg k10,500
2kg k4,500

Chimanga Popcorn, mtengo ndi:
500g - k4,000

For orders and delivery:
Call on:
+265 999 23 29 01


02/03/2026

Mpunga okoma wa TC 11 Kilombero ukupezeka.

Tiyimbireni pa 0999232901



16/02/2026

Kodi munaulawa mpunga wa TC11 Kilombero?

Tatiuzeni ndemanga yanu mu vomment section?


14/02/2026

Kuli masewera atsikana achitanyu pa Bingu Stadium masanawa pakati pa Malawi U-20 ndi Guinea Bissau
Mpirawu ndiwa ulele koma nkutheka mufuna
Popcorn
Mpunga
Ufa
Apa mwayandikira kuchimake kopezeka katunduyu wa TC 11

Tiyankhuleni pa 0 999 232 901


13/02/2026

Ndika mvula kameneka popcorn angakometu kumwera chai ☕️🍿

500g ali pa k4,000 yokha basi.

Tiyankhuleni pa 0999 232 901


13/02/2026

Awatu adya!
Alipo samafuna kudya?

Ndi k12,000 (2kg) kapena k30,000 (5kg) m***a kupeza wanu.

Tiyimbireni pa nambala iyi 👇

0 999 232 901


08/02/2026

Ma umboni akupitilira kuperekedwa....kodi inu zabwino ayi?

Gulani wanu lero mpunga, ufa (mgaiwa, oyera, gramil) ndi popcorn ndipo simuzakhumudwa.

Tiyankhuleni pa nambala iyi 👇

0999 23 29 01


06/02/2026

Mukudikira mpunga kapena nsima or phala, palitu Popcorn wa quality!

Tayimbani pa nambala ili mmunsi kuti mupeze wanu pa mtengo wa ziiii.

500g pa k4,000

Call: 0999232901


03/02/2026

Kodi mwawagulira kale Popcorn wa TC 11 anawo?
Nthawi yama cartoon yakwana yokha...

Gulani wanu pa mtengo wa:
K4,000 packet ya 500g

Tiyimbireni pa:
0999 23 29 01


Photos from Choyamba, Tidye's post 03/02/2026

Anzanu akugula and akuchitira umboni za makomedwe ake.

Gulani wanu lero ndipo muzazindikira kuti mumachedwa.

Timaperekera madera amu Lilongwe komanso kutumiza kunja kwa Lilongwe.

Mpunga wa Kilombero, mtengo ndi:
5kg - k30,000
2kg - k12,000

Ufa wa gaiwa, gramil ndi oyera wama vitamins ndima Minerals uliponso.

Mtengo:
5kg k10,500
2kg k4,500

Chimanga Popcorn, mtengo ndi:
500g - k4,000

For orders and delivery:
Call on:
+265 999 23 29 01




Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Mzuzu?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Culinary Team

Attire

Website

Address

Mzuzu
GULLIVERAREA49