11/11/2025
Christiano RONALDO wanena kuti 2026 World cup ikhala yomaliza kumenya mu mpikisano umenewu wa World cup chifukwa alibe zaka Zambiri akusewerabe mpira.
Sharing news abut football is our aim ⚽ ⚽ ⚽ ⚽ ⚽
11/11/2025
Christiano RONALDO wanena kuti 2026 World cup ikhala yomaliza kumenya mu mpikisano umenewu wa World cup chifukwa alibe zaka Zambiri akusewerabe mpira.
11/11/2025
Arsenal next 3 fixtures koma akungi anthuwa apwetekana awa.
11/11/2025
No player has made more interceptions than Moisés Caicedo (26) in the Premier League this season.
Akungi mukuona bwa? Ichi tidya nacho bwinotu
11/11/2025
Since the start of this season BRENTFORD ndiyo yagoletsa zigoli za mbiri(9) from throw-in.
Koma awa apweteka ma team.
11/11/2025
LIVERPOOL manager ARNE SLOT Wang'ambitsa kale ma TICKET akungi kuposa ndi mene anang'ambitsira season yonse yathayi.
Akungi Koma ziyendapo apa?
11/11/2025
Ichichi chafika ndi Ma Set avutawa.
Akungi Nyimbo ikhale Ma Set
10/11/2025
Zoti Akusewera mpira zosawakhuza ayi ndithu Kudya Apple FODEN and HALAAND.
Real meaning of Phweteko
10/11/2025
Akungi akuti sakuchotsa tsitsi mpaka FLORIAN WIRTZ atagoletsa Premier league goal komatu akungi.
10/11/2025
Kwacha bwanj akungi tiyeni tiyeseso.
Koma ichichi anthu akuchitama kuti chadyetsa bwino anthu.
09/11/2025
FT: MANCHESTER CITY 3-0 LIVERPOOL
After week 11 in EPL yanu ili pat?
63' Khooooo!!!!!! DOKU!!! MAN CITY 3-0 LIVERPOOL
HT: MANCHESTER CITY 2-0 LIVERPOOL