Nsanama Football Lovers Page

Nsanama Football Lovers Page

Share

Sports venue..where u can let people about sports

10/12/2025

Umu ndi mene zikutendera mu league yaku m'mawa kwa dziko lino

30/07/2025

Umu ndi mene ma team akuyendera mu mpikisano wa Durata division one league ku Eastern Region

15/07/2025

Umu ndi mene log table ikuyendera ku Eastern Region Football Association - Let them play Durata Division one league

Ndipo ma team onse awiri Ali ndi masewero awo a #6 kumathero a sabata ino

Loweluka Nsanama Young Soccer SC ikupita ku Balaka komwe ikukakumana ndi Milanzi malawitunes pa balaka secondary school ground

Lamulungu Mari admark lions yaitanisa anyamata aku salabani omwe ndi Ululu fc pa mgodi ground

Tikuyenera kuwafunira zabwino zonse ma team athu onse awiri pamene akusaka chipambano ndi 3 points kumathero a sabatayi

08/07/2025

Umu ndi mene ma team atengeselana mu Division one

06/07/2025

Mwaswera bwanji masana ano
Pamene League ya Durata division one yafika masabata asanu (5)
Ma team athu sabata ino akusewera masewelo awo a #4
Dzulo Nsanama Young Soccer SC inayenda kupita ku balaka ku mwima komwe akagonjesa anyamata a Jihad fc 4-1 pakwao

Lero Mari admark yaitanisa anyamata aku Chilumba Cha chisi chomwe chili pa nyanja ya chirwa ku Zomba yomwe ndi Muluma fc masana ano pa mgodi ground


21/06/2025

Eastern Region Durata Division one league

Team ya Nsanama lero inali ndi masewero achiwiri mu leagueyi pamene yagonjesa anyamata azachitetezo chama boda, owona zolowa ndizotuluka aku Zomba
Zomba Immigration, pa police ground
Chigoli Cha Bashir chomwe chinabwera pa mphindi 7 zoyambilira komanso Simion yemwe anakhoma nsomali omaliza pa mphindi zowonjezera kuti masewelowa athe,

Davie Banda Junior yemwe anali katswiri omwesa zigoli wakale.ku team ya Nsanama fc ndipo anakhalapo Dolo oziwa kumwesa zigoli mu Chitetezo mbaula southern region Division one League 2015 season atamwesa zigoli 51 pa masewero okwana 38 onse a season imeneo, anawayendera anyamata ndikuwalimbikisa anyamata kuti ayike gear ina kuti mwina azamalize pa number yabwino

14/06/2025

Results and Log Table For EASTERN REGION FOOTBALL ASSOCIATION (ERFA)
DURATA DIVISION ONE LEAGUE

WEEK2

14 JUNE SATURDAY

Milanzi Malawi Tunes 0-5 Jihad
William Anusa ( 5goals)

Kababa Academy 3-0 Mali Admarc
Charles Alli
Fortune Thauka
Hanniff Allen

Letico 0-3 Immigration
Gift Pillow
Kumbukani Chikoko(brace)



10/06/2025

Eastern Region Football Association - Let them play
Durata Division one fixtures

Saturday 14 June 2025
fc vs
Venue: chikowi ground Zomba

Sunday 15 June 2025
Nsanama Young soccer vs Buffaloes fc
Venue: Mgodi ground
Mtengo: K500 pakhomo

Pamene League yayamba, ma teams onse awiri apa mudzi pano Ali ndi masewero awo kumathero a sabatayi pamene Mari admark ikuyenda kupita kuzomba siku losatila lakelo Nsanama Young soccer ikuyamba ndipakhomo

Tiyeni tiwapase sapoti ma teams onsewa

09/06/2025

Meet our coaches of Nsanama teams which are participating in Division one league

Left Wilson kalino of Mari admark lions
Right Benjamin munyewe of Nsanama young soccer

09/06/2025

Good morning to all football lovers
The waiting moment is now over, as yesterday ERFA has launched the Division one league in mpasa cdss ground phalombe, where mukhota fc from phalombe hosted ululu fc from machinga District,
The match ended 1 all draw,
The visiting team scored in the added minutes of the first half, while the home team equalises in the second half.
As we start the League, let's support our teams by filling up the spaces at mgodi ground
Your presence and support at the ground will surely give them support and motivation
Don't forget we have
and which will represent our area and being in the 4 teams which will represent machinga District,
That also include and which were in action yesterday's game at pholombe

The charges at the gate will be K500 each, every game
Your support will highly be appreciated

We will keep updated with the fixtures and results as the League commence

04/06/2025

FRIENDLY GAME UPDATE

Kanjeza fc vs Nsanama Young soccer

Malo: kanjeza school ground
Siku: lero pa 4 June ( lachitatu)

Tikhala tikukupasilani zosatila

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Machinga?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Telephone

Website

Address

Nsanama Machinga
Machinga