13/06/2026
Zokozekera Zomaliza Pa Bingu. β
Bullets yakonzeka kusewera quarterfinal ya Airtel Top 8 usikuuno motsutsana ndi Ekhaya FC pa Bingu National Stadium.
π ππ πππππ πππ πππππππ π πππ πππ'π ππππππ ππππ οΏ½οΏ½ β€οΈβ¨οΈπ₯β¨οΈβ€οΈβ¨οΈπ²πΌπ²πΌπ²πΌοΏ½οΏ½
13/06/2026
Zokozekera Zomaliza Pa Bingu. β
Bullets yakonzeka kusewera quarterfinal ya Airtel Top 8 usikuuno motsutsana ndi Ekhaya FC pa Bingu National Stadium.
13/06/2026
ββββββββββ ITS ββββββββββ
MATCH DAY
Come Out And Support THE PEOPLE'S TEAM!
FCB Nyasa Big Bullets v Ekhaya FC
π Airtel Top 8 QF1
ποΈ Bingu National Stadium
π 5:00PM
11/06/2026
π¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉπ¦πΉ
ποΈNditha kukuuzani pano kuti mphunzitsi wamkulu watimu ya FCB Nyasa Big Bullets Fc Witson Wedson Nyirenda wafika kale pa ground lero pomwe anali ndi nthawi yapadera yodziwana ndi osewera ake. Mphunzitsiyu yemwe dzulo wasainira contract yazaka ziwiri ndi Bullets wati ntchito yake yoyamba ndikubwezeretsa kuzikhulupilira mwa osewera (Confidence) komaso mtima ofuna kupambana masewero alionse.
ποΈ Poyankhula zamasomphenya ake, Wedson Nyirenda wati akuona kuti timuyi osewera abwino alipo kale koma chomwe chufunika mkuwalimbikitsa komaso kuwapatsa chikhulupiliro kuti atha kuchita bwino monga osewera atimu iliyonse.
π€Mmene ilili mbiri ya Bullets Fc,zikuchita kuonetseratu kuti timuyi inazolowera kuwina zikho ndipo chimenechi ndichimodxi mwazifukwa zomwe zinandipangitsa kuti ndiganize zophunzitsa timuyi imeneyi. Kuwina ligi ndikhumbo langa komaso mmene ilili Bullets nkhani yowina ligi siyochita kukambirana chifukwa ndi chikhalidwe chake. ποΈwayankhula motero mphunzitsi watsopano watimuyi a Wedson Nyirenda.
ποΈPali chiyembekezo choti mphunzitsiyu akhale akutsogolera timuyi masewero omwe alipo loweruka likubwerali pomwe Bullets ikuyembekezeka kusewera nditimu ya Ekhaya Fc muchikho cha Airtel Top8 pa Bingu National Stadium ποΈ. Izi zikuyembekezereka kuchitika mothandizidwa ndi achina Heston Munthali omwe akhala nayo timuyi kufikira pomwe a Nyirenda alengezedwa kuti ndikochi wa Bullets.
ποΈThe PeoplesTeam yapanga zokonzekera zake zomaliza munzinda wa Blantyre pomwe mawa ikuyembekezeka kunyamuka kumapita ku Lilongwe komwe ikapitilize zokonzekera zake isanakumane ndi anyamata a Ekhaya Fc loweruka pa 13 June. Pa ground lero pamaoneka motere
GOALKEEPERS
β½β½β½β½β½β½
McLean Mwale
Pilirani Mapira
Julius Banda
Innocent Nyasulu
DEFENDER'S
β½β½β½β½β½β½
Edward Thengo
Yamikani Mologeni
Henry Chiwaya
Aaron Chilipa
Blessings Mpokera
Andrew Jovinala
Emanuel Kaunga
Khumbo Banda
MIDFIELDER
β½β½β½β½β½β½
Mike Mkwate
Madalitso Safuli
Peter Banda
Frank Willard
Wongani Lungu
Chawanangwa Gumbo
Prince Chiumia
Misheck Billiat
Clever Kalambo
Sean McBrams
STRIKERS
β½β½β½β½β½β½
Gasten Phodo
George Chaomba
Hassan Kajoke
Dastan Banda
ποΈ Madzulo abwino Mapale kulikonse komwe muli timakunyadirani π π
ποΈ
Maule4Life β€οΈ β½ β½ β€οΈ
11/06/2026
π Back In Action.
Ma quarterfinals a Airtel Top 8 akudikira. ππΎ
Let's Gooo Mapaleeeeeeeeeeeeeeeh
10/06/2026
πHERE WE GOOOOOO π
Timu ya FCB Nyasa Big Bullets yasankha a Wedson Nyirenda aku Zambia ngati mphunzitsi watsopano wa timuyi.
A Nyirenda omwe anakhalako mphunzitsi wamkulu watimu ya masewero a mpira ku Zambia, awalandira pa msonkhano wa atolankhani ku Blantyre masanawa.
Wedson Nyirenda watikitira contract yadzaka ziwiri ndi team ya FCB Nyasa Big Bullets β€οΈ
10/06/2026
BIG DAY AT BULLETSπ€
FCB Nyasa Big Bullets are expected to unveil their*new head coach this afternoon at their offices in Blantyre, as reported on Saturday.
Nothing changes. Itβs just a matter of time.
Itβs time for Wada Wada! Already introduced to the players and deal already signed.
08/06/2026
Timu ya FCB Nyasa Big Bullets FC yatenga katswiri wa mpira wa miyendo wa mdziko la Zambia Mphunzisi Wilson Nyirenda ngati mphunzisi wamkulu wa timuyi.
Malingana ndi mgwirizano wa pakati pa timuyi ndi Mphunzisi Nyirenda iyeyu akuyenera kubwera ndi anthu ogwira ntchito ake ochokeraso mdzikolo.
Mphunzisiyu waphunzitsapo matimu osiyanasiyana monga Zanaco, Zesco komanso matimu akuluakulu mdziko la Mozambique komanso South Africa. Mphunzisi Nyirenda watenga zikho zikuluzikulu zisanu ndi zitatu mmayikowo.
05/06/2026
π¨Mapemba is Back indeedπ―
Nkhani yabwino kwa mapalestina tsopano ndiyakuti osewera wathu wakumbuyo koma chakumanzele Crispine watatao mapemba tsopano wayamba kuchita zokonzekela ndi anzake ndipo ali pa mlingo uti atha kusewera masewero pakadali pano koma mwina sangamalize 90 minutsπ―
Maule mwamulandila bwanji mapemba pamene wabwela ma team atamange tsopanoπ Bwalo La Mapale - Maule Fans follow for more FCB sports news
31/05/2026
Sizikukongola ku family ya Mapale ππππππππππππππππππππππππππππππππππππππππππππππ
6 games 2 wins 4 draws 10 points
31/05/2026
π²πΌ MALAWI : FDH Bank PremierShip
FCB Nyasa Big Bullets v Moyale Barracks
β±οΈ14:30
ποΈ Joice Chitsulo Stadium
Goshen City Dedza Dynamons v Kamuzu Barracks
β±οΈ14:30
ποΈ Dedza Stadium
Chitipa United v Mighty Wanderers
β±οΈ14:30
ποΈ Chitipa Stadium
Karonga United v Red Lions
β±οΈ14:30
ποΈ Karonga Stadium
Follow Us Bwalo La Mapale - Maule Fans for more sports news
π