29/11/2023
Ma********on (kubunyula kuzigona wekha)
Ma********on ndi mchitidwe oipa kwambiri umene achinyamata akumanga masiku ano pongofuna kuzisangalatsa mwa iwo okha koma ziwani kuti mchitidwe umeneu ndi ochokela kwa satana pongofuna kumutalikisani ndi mulungu komaso kukugwilitsa ntchito pa zofuna zake
Kodi ndizoipa bwanj?
Kubunyula ndi chimo komaso kumaononga umoyo wa munthu chifukwa munthu amene wazolowela kubunyula amazazidwa ndi ziwanda zimene zimamulamulira kotelo samakhumba zogona ndi mkazi/ mamuna coz ziwanda zimenez zimakhala za nsanje . Kotelo kupeza mkazi/mamuna wachibwez/banja silimachedw kutha.
Komaso ukazolowela mchitidwe umeneu kugona ndi mkazi sumava kathu chifukwa pathawi yomwe ukubunyula manja amakhala ulimba kotelo misepha ya chida chanu imakhala ikupelepeseka!
Ziwanda zimenez zimakhala zikuyamwa ma s***m pa thawi imeneyi kumapitisa kumidima kumakapangila zofuna zawo.
Zikatelo umakhala munthu osowa mtendele mmoyo wako komaso zimalanda mwayi wako kukusiya uli mmavuto azaoneni
27/11/2023
Tiseke pang'ono!
Musa : hello ; amayi ndikufuna ndizibwela kumeneko ku Jon kuno andipeza ndi matenda a HIV/AIDS
Mayi: ayi usabwele mwana wanga
Musa: amayi bwanji mukundilesa kubwela?
Mayi: Mesa wati akupeza ndi HIV/AIDS
Musa: eya!
Mayi : kungoti ukabwela uza mpasila mkazi wako mkazi wako aza mpasila mchimwene wako mchimwene wako wako aza mpasila wa ntchito uja wa ntchito azapasila bambo ako mbambo ako azandipasila ineyo ineyo ndizapasila gate man gate man azampasila mchemwali wako chemwali wako azampasila mudzi onse . Chonde miyoyo yathu ili mmanja mwakoπ€π€π€
06/11/2023
Morning fan . Ndafuna kukuziwitsani kuti ndikufuna ndipange WhatsApp group kuti ndikayamba kukupasilani khani zisamakuphonyeni coz Pali zambiri zoti ndikupasileni ngakhale zikundivuta kuti ndiziyambe chifukwa Cha ma busy koma I hope zitheka ndimakunyadilani nonseππ―πππ
09/10/2023
MAZULO NDIBWELA NDI KHANI YA KUIPA KWA MUSTURBATION ( KUBUNYULA).
ZOMWE ZIMAYAMBISA NDIKUYIPA KWAKe .
BE THERE AROUND 7:30
08/10/2023
Hello , ma followers nonse konse komwe muli tithokoze mulungu potipangisa kukumanaso lero. Ndinasowa mwa kathawi ndithu pazifukwa Zina zinandipinga koma kungothokoza kuti tili ndi moyo . Tiyambekuyendela limozi pa khani zathu kuyambila mawa zikomoπΎππ
12/07/2023
Banana and water after running it's important
12/07/2023
Ulendo Uno kulibe kuloweza nyimbo za driemo wa imba mchizungu mwene even ma Tik Tok muli Ziπππππ
11/07/2023
Vuto mamuna oti angakusamale samakhala ndi fundo zeni Zen Koma atabwaliwa fundo imodzi kutholera Khosi !
07/07/2023
From inbox!:
Kodi guys mwamuna kupeza ndalama Koma si ya salary ndikumuonesa mkazi mkulakwa?
07/07/2023
Chikond chomwechi ena aziwa nacho maiko ena kugulilidwa Malo ena achosedwa nacho Mano ena mpaka BP kukwela! Inu muli Pati?π§π§π§π§
28/06/2023
Mowa omwesedwa inu mpaka kutenga cha phepo. Wakuuzan ndani kuti mukachezeraπ§π§π§