Zkavuta kubanjakotu kumabwelera
Family & Dates advice
Sports updates, transfers and results
Mtsikana yemwe dzina lake ndi Sabina wawomberedwa ndi boyfriend wake yemwe ndiwa police kenako iyeso wadziwomberaso, pakali pano matupi awo anyamulidwa kupita ku mortuary ya Dedza.
Malingana ndi ena omwe anayitsatira bwino nkhaniyi akuti Sabina dzuro amamwa mowa ndi anthu zomwe sizina musangalatse mamunayu.
Kucha kwa lero analawilira kunyumba kwa Sabina komwe atafika anafusa ma Neba ngati alipo ndipo anamuwuza kuti alipo. Apa iye anagogoda Sabina mkutsegura. Atalowa anayamba kukangana kenako mamuna anatulutsa mfuti mkumuwombera mkaziyu kawiri pa mtima kenako nayeso mkuziwomberaso.
After being on the bench for the first two games and not playing a single minute at the AFCON, Angola midfielder 🇦🇴 Beni Mukendi left camp and returned to his club Casa Pia in Portugal.
His first game back was an 8-0 loss to Sporting CP.
Mukendi played 86 minutes and was subbed off.
HUSBAND CALLS WIFE ON PHONE.
Husband: Where are you?
Wife : At home love.
Husband: Are you sure?
Wife: Yes.
Husband : Turn on the microwave.
Wife : (turns microwave on) Rrrreeereeeereeee...
Husband: Ok my love goodbye.
ANOTHER DAY......
$uspicious Husband: Where are you?
Wife: At home love.
Husband: Are you sure?
Wife : Yes.
Husband: Turn on the microwave.
Wife: (turns microwave on) Rrreeereeeereeee...
Husband: Ok my love goodbye.
The next day, the husband decides to call on his son's phone and he asks him, "Son, where is your mother?"
Son: "I don't know, she went out with the microwave 3days ago
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 👇
We are already at 100 goals in this African Cup Of Nations, which is as many as in AFCON 2021 and there are still 10 matches left. The record is 103 goals at the African Cup Of Nations 2019. 🍒❣🖤⚽️
This year's AFCON is just WOW
Koma mwat zkuchtikad zimeneziz
Wake him up, asambe then adye wa ku vephi
10/01/2024
Mnyamata wadzimangilira kamba kodzudzulidwa
Mnyamata wa zaka 18 zakubadwa yemwe anali mu fomu 1 wafa atadzinjatilira pa mtengo ku Mponela m'boma la Dowa kamba kakuti amadzudzulidwa pakhalidwe lake lochita maubwezi ndi atsikana osiyanasiyana.
Mnyamata wadzimangilira kamba kodzudzulidwa Malawi 24 | Latest News from Malawi Mnyamata wadzimangilira kamba kodzudzulidwa Malawi 24 | Latest News from Malawi | Stay up-to-date with the latest news from Malawi and around the world, 24/7.
Don't forget to call your loved ones
Morning family
Click here to claim your Sponsored Listing.