Malawi Soccer News,Fixtures Results 2019/2020 Season

Malawi Soccer News,Fixtures Results 2019/2020 Season

Official page for sports

28/07/2020

*WAKE UP CALL THIS MORNING*

*TUESDAY 28 JULY 2020*

*MWAGALAMUKA BWANJI A MALAWI NONSE OKONDA MASEWERO AMPIRA WA MIYENDO DZIKO MUNO??*

*Life Made Us Friends🔥🔥🔥But Football Made Us Brothers⚽⚽⚽❤💯🙏🏽🙏🏽And Football Bring Us Together🔥🔥🔥❤💪🏼💪🏼💯*

Boma komanso *Football Association of Malawi*(Fam) osaiwala *Super League of Malawi*(Sulom) akuyeneka kupeza njira yoti mpira uyambenso dziko muno ngakhale *Coronavirus*(Covid 19) wavuta kamba koti muliri uwu unabwera kuzakhala sukutha lero ngati zivute bungwe la *Football Association of Malawi*(Fam) komanso *Super League of Malawi*(Sulom) awauze ma team kuti apange maplayers ayendere yawo watero *Higger Mkandawire* mlembi wakale wa *Nyasa big bullets Fc*

Sitikuthamanga sitikuti or boma la *Malawi* litanena kuti mpira uyambe sizikutathauza kuti mpira uyamba mwenzi wa mawa koma akuyeneka ma team uzapasidwa mpata okwanira kuti akozeke watero *Football Association of Malawi*(Fam) president *Walter Nyamilandu* izi zaza kamba koti boma la dziko lino silikuonetsa chidwi choti mpira uyambe kamba koti pempho la *Football Association of Malawi*(Fam) silinayakhidwe

Nditha kuuzani kuti *Kamuzu Stadium* silizapanga host ma game a *Caf* zomwe zikutathauza kuti masewero akayamba *Malawi* the *Flames* masewero ake azikaseweredwa pa *Bingu National Stadium*(BNS) izi zachitika kamba koti dziko la *Malawi* linatenga *Kamuzu Stadium* ngati malo a *Quarantine* miyezi yapitawo

Nditha kuuzani *Israel Kam'mwamba* amutulutsa ku ndende dzulo kusatira atamupanga bail *Israel Kam'mwamba* ndikatswiri waza nkhonya yemwe anazatenga malamulo manja mwake ndikumenya munthu

Ndateremu ndafika kumapeto kwa nkhan zamasewero mwakoma nonse zikomo Mulungu akudalitsen mukhale ndi tsiku lopambana

Ilira itayambika nkhondo yamwini savulira jacket@ *🇲🇼🇲🇼🇲🇼Mr Nyasaland Aka Technical reporter* mwana wa aunt naphiri *(Sp⚽rtsMan)* kuchokera ku *Chiradzulu* kwao kwa *John Chilembwe* mamawa wamampha ndaluta ✍🏼✍🏼✍🏼✍🏼✍🏼✍🏼✍🏼✍🏼✍🏼

17/07/2020

Pepani nonse ma followers a page ino coz mwakhala nthawi yayitali kopanda ma post aliwose pano ndabwereraso muchimake so be ready

26/05/2019

"Iam not going anywhere"says Mhango

Bidvest Wits have exercised the one-year option they had with Gabadinho Mhango

Mhango who is set to take part in the COSAFA cup game against Seychelles this afternoon in South Africa,only featured 12 times in the league for the Clever Boys in 2018/19 season

There was a strong belief that the 26-year-old might join Kaizer Chiefs next season,but with this latest development Amakhosi will now have to deep into their pockets if they are really interested in the player

"Iam not going anywhere"Mhango tells in South Africa

11/05/2019

Welcome & Tigers 0-2 Mlatho mponera

26/03/2019

Pali manong'onog'o oti FAM yaika pa list makochi four oti m'mozi mwa iwo akhoza kutenga mpando wa coach wa Frames anthuwa ndiawa

PATRICK MABEDI
KINAAH PHILI
EDI NG'ONAMO

KOMANSO CALISTO PASUWA emwe akukocha Bullets pakali pano

Kodi mwa onsewa amene akuoneka kuti akhonza kuisintha team yathu ya Frames angakhale ndani

Maganizo anu aonesa m'mene mumakondela dziko lanu

WAMAPAZI ⚽⚽⚽

05/03/2019

*WAKE UP CALL DIS MORNING*

*MWAGALAMUKA BWANJ AMALAWI NONSE OKONDA MASEWERO AMPIRA WA MIYENDO..............??????*

Team ya *Ferroviario de Nampula* ndiyomwe yakhala akatswiri a *Nyasa Challenge international bonanza* mu chaka cha *2019* kusatira ndikupanga draw kwa game ya *Ferroviario de Nampula vs Chicken Inn* komanso *Nyasa big bullets vs Beforward wonderers* ndizomwe zapangitsa *Ferroviario De Nampula* kuti akhale wa *Nyasa Challenge international bonanza*

Ma team onse a *Ferroviario de Nampula,Chicken Inn* komanso *Beforward wonderers Fc* ayamikira team ya *Nyasa big bullets Fc* popanga *Bonanza* yaikulu ngati imeneyi ndipo ma team amene ati next year ayesesa nawo azaike ndalama mu *Bonanza* imeneyi

*Nyasa Challenge international bonanza yesterday results*

Chicken Inn 1-1 Ferroviario de Nampula

Nyasa big bullets Fc 1-1 Beforward wonderers Fc

Ndalama zokwana *MK15,000,000,00* ndizomwe ma team a *Ferroviario de Nampula* komanso *Chicken Inn* aliyese watenga kupita nawo kwawo pomwe ma team a *Nyasa big bullets Fc* komanso *Beforward wonderers Fc* aliyese kwao wapita ndi *Mk10,000,000,00* mu bonanza yomwe inalipo

Ferroviario de Nampula *MK15,000,000,00*

Chicken Inn *MK15,000,000,00*

Beforward wonderers *MK10,000,000,00*

Nyasa big bullets Fc *MK10,000,000,00*

Team ya *Beforward wonderers Fc* kuzera kwa captain wawo *Alfred manyozo* wati bonanza yawathandiza kukoza molakwika komanso aphunzra zithu zingapo kuchokera kwa ma team a *Ferroviario De Nampula* komanso *Chicken Inn* watero the captain *Alfred Manyozo*

Akwanilitse zomwe analonjeza asanasakhidwe anthu osata mpira waku *Malawi* ayakhula izi kusatira ndizisankho zomwe zinachita saturday ku *Salima* ku bungwe la *SuperLeague of Malawi* (SULOM) kuti agwire ntchito yotamandika

*Abigail Mwafulirwa* katswiri osewera masewero achemberembaye mu team ya *Karonga Queens* wati sakupanga appeal pachigamulo chomwe bungwe la *Netball Association of Malawi* (NAM) yomwe chapereka kwa iye choti zaka zokwana

04/03/2019

*WAKE UP CALL DIS MORNING*

*MWAGALAMUKA BWANJI AMALAWI NONSE OKONDA MASEWERO AMPIRA WA MIYENDO????????*

Team ya *Malawi U23* yafika mwaphephe dziko la *Egypt* pomwe ikuchokera ku *Belgium* yasewera ma game okwana *6* yawina awiri yagonja kawiri yapanga draw yawiri *Malawi U23* asewera ndi *Egypt U23* lachisanu

Lero ndi tsiku la mtengo wapatali kwa wina aliyese okonda masewero ku mtundu wa bambo ndi mai *Malawi* pomwe *Nyasa Challenge international bonanza* yabwera ndi zithu ziwiri zosiyani mu *Blantyre derby* yoyamba mu *2019* pomwe ma team omwe saonana bwino a *Nyasa big bullets Fc* komanso *Beforward wonderers Fc* akhale akusosolana mthenga pa *Kamuzu Stadium* ndipo *Nyasa challenge international bonanza* ikutha lero koma mwai oti *Nyasa Challenge international bonanza* itha kutengedwa ndi *Ferroviario de Nampura* komanso *Beforward wonderers* chifukwa ali ndi ma points ochuluka

Kumano omwe unalipo zulo ku ma team a *Ferroviario de Nampura ,Chicken Inn* apempha *Nyasa big bullets Fc* kuti mpikisano wa *Nyasa Challenge international bonanza* izichitika chaka ndi chaka ndipo usasitha uzikhalira ku *Malawi* kuno ndipo ma team a *Ferroviario de Nampura* komanso *Chicken Inn* akuti ndiokozeka kumabwera chaka chilichonse ku *Malawi* ndipo akafika kwawo ma team amenewa akafikira ma company kuti aziwathandiza pobwera ku *Malawi*

*Nyasa Challenge international bonanza today fixture's*

*Monday 4th March 2019*

Ferroviario de Nampura vs Chicken Inn @ *Kamuzu stadium* 13:30hrs

*This is first Blantyre derby in 2019*
Nyasa big bullets Fc vs Beforward wonderers @ *Kamuzu stadium* 15:30hrs

Bungwe la *Football Association Of Malawi* (FAM) komanso *SuperLeague of Malawi* (SULOM) agwirizana kuti *Tnm SuperLeague 2019* izayambe pa *14 April 2019* ndipo ma *Fixture's* atuluka next week

Team ya *Mighty Tigers Fc* ikusendera chifupi ndi sponsorship yasopano koma team ya *Mighty Tigers Fc* sinaulure kuti ndi company iti yomwe ikufuna kutenga *Mighty Tigers Fc* yomwe pano ilibe

03/03/2019

*WAKE UP CALL DIS MORNING*

*MWAGALAMUKA BWANJI AMALAWI NONSE OKONDA MASEWERO AMPIRA WA MIYENDO.........??????*

*Nyasa big bullets Fc* yachita kuchokera kumbuyo kuumbuza team yaku *Zimbabwe* yotchedwa *Chicken Inn* team ya *Nyasa big bullets Fc* ithokoze *Henry Kabichi* komanso *Chiukepo Msowoya* kuti iphe mwakhaza ndmomvetsa chison *2-1*

Team ya *Beforward wonderers Fc* yachita kuchitaya yokha yokha pomwe yakanika kugonjetsa *Ferroviario de Nampura* masapota a *Beforward wonderers Fc* atha kumuimba mlandu *Mike Kaziputa* pomphonya penote komanso *Bongan Kaipa* pozichinya yenkha kuti mpira uthere *1-1*

*Nyasa Challenge international bonanza yesterday results*

Beforward 1-1 Ferreviario de Nampura *(Francisco's Madinga)* *(Own Goal Bongan Kaipa)*

Nyasa big bullets Fc 2-1 Chicken Inn *(Henry Kabichi & Chiukepo Msowoya)* *(Augusto)* *Nbb come from behind to beat Chicken inn*

Lero kulibe ma game amu *Nyasa challenge International Bonanza*

*Monday 4 March 2019*

Ferroviario de Nampura vs Chicken Inn@ *Kamuzu stadium* 13:00hrs

Nyasa big bullets Fc vs Beforward wonderers Fc@ *Kamuzu stadium* 15:00hrs

Bungwe la *Sulom* lili ndi khope zina zatsopano kusatra ndi zisankho zomwe zachitika dzulo ku *Salima*

*Super League Of Malawi (SULOM) New Executive Committee*

*President*
Tiya Somba Banda
*Vice President*
Gift Mitawa
*General Secretary*
Williams Banda
*Vice General Secretary*
Zakalia Nyirenda
*Legal Advisor*
Muhammad Selemani
*Treasure*
Malinda Chinyama
*Executive members*
Charles Manyungwa
Chimzy Nyirenda
Allie Mwachande
Henry Banda
Michael Chemayere

*FAM* Serious with connect roll out *Fam* continues training its stakeholder in operations of the mpira connect platform an online football stakeholders registration platform

The Association has made online resignation mandatory 2019

On Saturday *Fam* trained about 25 central regional officials from Various Regional commitee namely *referees,Coaches women* and beach soccer

So far about *80* people have bee

27/02/2019

Crystal palice 0-2 Man united
Arsenal 4-1inayo

27/02/2019

BACK TO MY ROOTS!

Emanuel Zoya wabwelera ku timu ya Civil Sporting pomwe wasayina contract ya zaka ziwiri kutsatira kutha kwa contract yake ku Nyasa Big Bullets...

Feel at home Ambewe!

Sports Master

27/02/2019

*OSAONETSA KUTOPA, KOMANSO OSAFOOKA NDILANDIRENI INE SIR-ALEX M'MAWA A LERO PA (27/02/19) PAMENE NDABWERANSO NDI NKHANI ZA MASEWERO*✍🏻 🇦🇹🇦🇹 ⚽🤾‍♀
-------------------------------
Msalamangwe posatira nkhani za masewero mdziko muno zayamikira akulu-akulu a *Company* ya *NMC,* omwe ndi ayini ake ateam ya 🅱🅱ullets.
Pa chiganizo chomwe achita, chotitsa *International Bonanza.*

Zatero msalamangwezi, zomwe ndi *Dr Kaponda Masiye, Lenard Shawa,* ndi *Charles Grand-Master Nyirenda.*
Msalamangwe zitatu-zi, zinawonjezeranso kuti-- *International Bonanza* imeneyi yomwe iyambe lachisanu limene likubwelari pa (1st March 2019) yabwera mu nthawi yabwino, chifukwa chakuti ma team awiri amene akubwera a *De Nampura,* ya ku *Mozambique,* ndi *Chicken Inn* ya ku *Zimbabwe,* ndi team akulu-akulu amene amachitanso bwino mu *league* yainkulu ya maiko awo.
.......Iwo anati--mwachitsanzo *De Nampula,* yaku *Mozambique* inamaliza pa #3 mu *league* ya kwao.
pomwe team ya mdziko la *Zimbabwe* ya *Chicken Inn* inamalidza pa #2 kusonyodza kuti mateam awiri amenewa simateam achibwana ayi.

Komanso tikuyenera timubvulire chipewa, mkulu wa team ya *Bullets, Fleetwood haiya* zikuonetsa kuti munthuyu ndi katakwe kwambiri pankhani yoyendetsa team yake, ndipodi akuyendetsadi team-yi mwa *business,* kuyika pa k**a ndalama yokwana(K50, million) yopangitsira *International Bonanza* sichinthu chamasewera atha pang'ono ndi ndime yainkuru ndithu.

Komanso timuyamikire pomutenga *Neba* wake kuti asewere nawo mu *Bonanza,* imeneyi.
Iwo anati, mwezi wathau unathetsedwa ubare pakati pa ma team awiri amenewa, ndipo chomwe chinatsitsa zaye kuti njobvu ithyoke mnyanga ndi nkhani ya *Precious Sambani,* yemwe anapita kwa neba wawo wa *Bullets,* izi zinapangitsa kuti akulu-akulu team ya *Mighty beforward wanders,* athetse ubare wao ndi team ya *NMC*🅱🅱 *Fc limited.*
Komano akulu-akulu a team ya *Bullets,* sanazitengere izi amuyitana neba wawo umenewo ndiye ubarewo.
Pakufunika kuti akulu-akulu a te

26/02/2019

*WAKE UP CALL THIS MORNING*

*MWAGALAMUKA BWANJ AMALAWI NONSE OKONDA MASEWERO AMPIRA WA MIYENDO?????*

Team ya *Nyasa big bullets Fc* yati chilichonse chokhuza bonanza yomwe iyambe *Friday* chatheka ndipo ma team a *De Nampura* yaku *Mozambique* komanso *Chicken Inn* yaku *Zimbabwe* afika *Thursay* masana ndipo ndalama zokwana *MK50,000,000,00* ndizomwe *Nyasa Manufacturing Company Ltd* yaika pa tebulo kuti ma team a *Chicken inn* komanso *De Nampura* agwiritse ntchito pogona kudya ndi mayende izi wanena ndi *Kelvin Moyo* marketing manager

Team ya *Beforward wonderers Fc* yakhazikitsa commitee yapadera yoti iziyang'ana ma contract ama player izi waulura ndi *Gift Mkandawire* nditafufuza ku team ya *Beforward wonderers Fc* ndapeza kuti ma player okwana *7* odalilika ku team ya *Beforward wonderers Fc* pofika mwenz wa mawa akhala *Free Agent* koma *Gift Mkandawire* wati ayesesa kuti onse omwe ma contract awo afika kumapeto awasaina

Team ya *Malawi U23* ikuyeneka kuganiza bwino pomwe ikuzakumana ndi team ya *Zambia U23* pomwe dzulo yagonjanso kachikena ndi team ya *Oud Heverlee Leuven* (OHL) ya ziko la *Belgium* komwe ikupanga camp kumeneko *Malawi U23* zulo inapereka chilimbikitso pobweza chigoli kuzera mwa *Chimzy Idana* koma pakuti gona kuphe sanali kutali ndi *Malawi U23* inachinyitsanso zigoli zina kuti pokutha pa *90Mins* *Oud Heverlee Leuven 3-1 Malawi U23*

Ma player a *Karonga Utd* ayamba kaye aima kupanga training kamba koti akulu a *Karonga Utd* sanapereke ndalama kwama player kufusa kwa *Lufeyo Chipanga Banda* wakana kuyakhulapo za nkhani imeneyi

Team ya *Mtopwa Utd* yati sikulembanso ntchito wachiwiri kwa mphunzitsi malingaliro a *Mtopwa Utd* anali pa *Eliya Guardiola Kananj* koma zithu sizinali chomwecho kamba koti mtima wazako ndi sidya lina *Eliya Kananji* ali ku *Master Security Fc* nditamufusa *Isaac Jomo Osman* wati teamy sikusitha technical panel ndipo iyenso azithandiza nawo pansi pa *Leo Ferguson Mpulura* ndipo *Mtopwa Utd* home ground yawo

25/02/2019

*Zampira koma Moyepula*

Ma player a team ya *Karonga Utd* ayamba anyanyala zokozekera za *2019* season pomwe auza akulu akulu ateam kuti awapatse zawo kafukufuku akuonetsa kuti ndalama za season ya *2018* ma player sanalandire zomwe zapangitse ma player aime kaye osamapanga training

Zitengera *Calisto Pasuwa* kusakha omwe agwire nawo ntchito season ino ngati omuthandizra ake pomwe zamveka kuti pokutha week ino apereke contract kwa technical panel koma pali chiopsezo chakuti *Calisto Pasuwa* ena amu technical panel sakuwafuna

Tsogolo la *M***a Manyenje* ku banja la *Nyasa big bullets Fc* sili kuoneka kamba koti akulu akulu a *Nyasa big bullets Fc* sanakambepo kathu zakusala pang'ono kutha kwa contract ya *M***a Manyenje* malipoti akuonetsa kuti pofika sunday *M***a Manyenje* akhala free agent

Tikulimba mtima kuti season ino ndi yathu ndipo tiyesesa kuti titenge zikho zingapo yatero team ya *Beforward wonderers Fc* kuzera mwa mlembi wa teamy *Gift Mkandawire*

*Stanley Sanud* pochoka ku *Belgium* akhala alibe team kamba koti contract yake ikutha pa *28 Feb 2018* ik**azati *00:00am* izakhala contract ya *Stanley Sanudi* itatha ndi *Beforward wonderers Fc* olo akulu akulu a team ya *Beforward wonderers Fc* akukanapo kuti contract ya *Stanley Sanudi* ndi yachikhalire

Zomwe ndnali nazo masana uno ndi zomwezi mwakoma nonse mukhale ndi masana mwanyatwa mulungu akudalitsen

*🇲🇼🇲🇼🇲🇼Mr Nyasaland Aka Technical reporter* mwana wa aunt naphiri Kundimaka ndikufuna kwako ndapita

08/02/2019

*Ndabweranso Ndi Stanley Sanudi*

Iyi ndi nkhondo yosayamba koma ngati *Nyasa big bullets Fc* ikufuna nkhondo inene mwanayu akupopedwa ndi akulu akulu a *Nyasa big bullets Fc* kuli chikulirano ku *Beforward Wonderers Fc* inu zikuti bwanj kusatira ndi ndikukana kusaina kwa *Stanley Sanud* ku *Beforward wonderers Fc* kukuutsa mapilire pa chigawo ndipo ngati *Nyasa big bullets Fc* itenge *Stanley Sanud* ayembekeze nkhondo yosaneneka tikuikumbutsanso *Nyasa big bullets Fc* ndiife sitimatengerana player ndipo ubale unatha izi ndizomwe ndapeza akukambirana akulu akulu a *Beforward wonderers Fc* wathu maliro kwao maliro therad kasiya mbamba *Stanley Sanudi* abweretsa chisokonezo

Ena akuti *Stanley Sanudi* let him gooo ndati *Stanley sanudi* akufuna dipo yochuluka kwambiri ku *Beforward wonderers Fc* inu inu *MK6,000,000,00* yachepa ine ndkufuna *MK7,000,000,00* ngati *Signing on feee* komanso ndizilandirandera *MK700,000,00* kupotsa *Babatunde Adeboye* apo biiiiiiiii sindkukhala kuno wanga ndamanga kale inu *🇲🇼🇲🇼🇲🇼Mr Nyasaland Aka Technical reporter* wakuuzan ndani inu ine sindmazimandira kapena kuzipopa ai sindmasangalatsa munthu ofuna ndmusangalatse nkhan sindimaonjera kapena kulemba nkhan yomwe ine sindikuziwa

Nkhan ndi yakuti *Stanley Sanudi* contract yake ikutha pa *28 February 2019* tikufuna nthawi yake izatha *00:00am* koma *Beforward wonderers Fc* ikuti *Stanley Sanudi* ali ndi contract yomwe ikutha mu *2020* ndnafuna kupita ku *Football Association Of Malawi* kukamufusa *Casper Jangale* ndione form ya *Stanley Sanudi* ndli ndi mwai anandionetsa contract ya *Stanley Sanudi* mene ikuthera ndapeza ikutha mwenz uno

Sindnatope koma kulunjika ku *Beforward wonderers Fc* ndione contract form ya *Stanley Sanudi* ikuti bwanj anakaniza andifusa kuti ndiiwe ndan oky chabwino sindnatope ndinalunjika kwa mwini nkhani *Stanley Sanudi* ndione contract form yake inu *Stanley sanudi* amangoseka wakana kundionetsa anangondiuza ziwani zomwe mwamvazo ndato oky chabwi

08/02/2019

.
KU MANOMA KWAVUTA INU MADZI ACHITA KATONDO SANGAMWEKESO AYI


*COPIED KUSELIKU*👇SANUDI

Akana kutikitila contract ina ku WANDERERS pomwe contract yake ndi team ya manoma ikutha pa 28 mwezi uno.

Akulu akulu a WANDERERS akuyesela kumuchondelela ndi 6 million kwacha koma SANUDI akuti akufuna 7 million kwacha komaso malipilo ake aduse mulingo wa BABATUNDE emwe akulandila 500,000 kwacha pano akulu akulu a team ya WANDERERS mitu yauma kuti njiii kosowa chochita .

Phekesela zikumveka kuti SANUDI maganizo ake ali ku NYASA BIG BULLETS..

MANOMA AZANGA NONSE AKULUAKULUWA AKUTIPUSISA HEAVY ZANAZANALI ANATIUZA KUTI SANUDI CONTRACT YAKE IKUTHA MU 2020 KODI INO NDI 2020????

ASATIPUSISE SANUDI WAUTALI KU NBB KHULUPILIRANI MANOMA.


*ABITI MANOMA*NOMA FANS RESPONSE

[10:13, 2019/02/08] ‪+27 84 216 2368‬: Amene mungathe kufotokoza bwino koma moveka bwino komaso mwachilungamo pankhani ya sanud .

Kodi akukana kusainaso

Kodi ifeyo ngati nyerere tidziwe ziti za sanud

[10:32, 2019/02/08] ‪+265 884 09 66 24‬: Eish wakulu amatha ndipo kuchoka kwaiyeyo eish ndizowawa bwanji[11:09, 2019/02/08] Wizzy Waxy: *Tikufuna mpira wathu ife Angozo osati Sanudi iye uja si Mr wanderers ayi ngati akuchoka apite komwe mtima wake uli basi*

[11:10, 2019/02/08] Hope Walker JNR: Kk*kk*k relo limenelo k*kk ndiponye ukazitape kodi haahahahahaha

[11:10, 2019/02/08] Hope Walker JNR: Wizzy koma munakanena kuti NGOZO u were right atleast for once k*kk*kk

[11:11, 2019/02/08] fatsani: Kk*kkk koma kumeneko...... odi ndikabibe ine🤣🤣🤣🤣

[11:11, 2019/02/08] Hope Walker JNR: Kkkakakakakakakak k*kjk*k

[11:12, 2019/02/08] songwe: Taponyani ndithu tione nao k*k

[11:13, 2019/02/08] Wizzy Waxy: *Angozo player aliyese ali ndi ufulu opita komwe akufuna nde ngati wakonda kutelo apite ndizampira basi iye uja ndi player wabwino kwambiri koma team ikhalapobe basi*

[11:13, 2019/02/08] fatsani: Mawu 🤣🤣🤣LIVE WIRE RESPONSE

Koma pa dzana paja m

08/02/2019

SANUDI

Akana kutikitila contract ina ku WANDERERS pomwe contract yake ndi team ya manoma ikutha pa 28 mwezi uno.

Akulu akulu a WANDERERS akuyesela kumuchondelela ndi 6 million kwacha koma SANUDI akuti akufuna 7 million kwacha komaso malipilo ake aguse mulingo wa BABATUNDE emwe akulandila 500,000 kwacha pano akulu akulu a team ya WANDERERS mitu yauma kuti njiii kosowa chochita .

Phekesela zikumveka kuti SANUDI maganizo ake ali ku NYASA BIG BULLETS..

MANOMA AZANGA NONSE AKULUAKULUWA AKUTIPUSISA HEAVY ZANAZANALI ANATIUZA KUTI SANUDI CONTRACT YAKE IKUTHA MU 2020 KODI INO NDI 2020????

ASATIPUSISE SANUDI WAUTALI KU NBB KHULUPILIRANI MANOMA.

*ABITI MANOMA*

08/02/2019

*Wake Up call this Morning*

*Mwagalamuka bwanji nonse okonda masewero ampira wa Miyendo??????*

Team ya *Azam tigers Fc* pano yasitha zina izitchedwa *Mighty Tigers Fc* kusatire ndikutha kwa ubale wa team ndi company ya *Bakhresa* izi zaziwika zulo ndinafuna kumva kuchokera kwa *Roben Abambo Alufandika* ngati nkhani yositha zina iliyoona iye wati ndizoona team ya *Azam tigers Fc* pano izitchedwa *Mighty Tigers*

Zochozekera za bonanza zayenda bwino chigawo chakumpoto malinga ndi akulu oyendetsa bonanza yemwenso ndi mlembi wa *Mzun Fc* *Donnex* ndipo bonanza ili mawa kutha Sunday

Nditha kuuzani kuti zoti *Prescious Sambani* anavulala ndizoona koma injury yake ndiyochepa chabe ndipo mu camp ya *Malawi U23* sanatuluke ali mu camp momo koma zokuti injury ya *Prescious Sambani* ndi ya *9months* ilo ndi bodza chabe

CEO wa *Nyasa big bullets Fc* *Fleetwood Haiya* wabwerezanso mau ake oti pofika next week diffender mbambande yemwe amatumikira malawi national team akhala atamusaina koma wakana kumutchula zina lake koma *Fleetwood Haiya* wangoti team ya mphangala imeneyo ili mu top 8

Mphangala ya *Silver Strikers Fc* *Green Harawa* zulo wachita ngozi ya galimoto pomwe pano ali ku chipatala ndnafuna kucheza ndi achibale ake a *Green Harawa* koma ma 4n awo pa nthawi yomwe ndimaimba samapezeka ndiye sindinathe kufusa kuti injury yake ndi yaikulu bwanji koma kafukufuku akuonetsa ndiyocepa chabe

Ma team ochokera zigawo chakumwera kumpoto komanso mpakati osaiwalanso *Under 20* akukumana mawa pa *Bingu Stadium* ndipo *Football Association of Malawi* yati mpikisano umenewu uzichitika chaka ndi chaka poyakhula ndi mphunzitsi wa team yakumwera *Leo Ferguson Mpulula* wati team yake yakozeka kuonetsa zakuda ma team omwe akukakumana nawo pa *Bingu national Stadium*

Kulephera kosalowa mu *Tnm SuperLeague* team ya *Nyasa big bullets resv* akulu akulu ateam anatchula team ya *Red Lions Fc* kuti isewere mu *Tnm SuperLeague* koma akulu akulu ena aku *FAM* anakana pempho la *Nyasa big

11/01/2018Kamuzu Baracks
Azam Tigers
Moyale Baracks
Tn Stars
Mzuni Fc
Nchalo United
Nyasa Big Bullets
Mafco
Karonga United
Master Security
Mighty Beforward Wanderes
Dwangwa United
Civil Sporting Club
Silver Strikers
Blue Eagles
Red Lions

Awa Ndi matimu 16 amene alimbane mu league ya tnm
yanu yilipo?

11/01/2018

rightous banda wasayina contract yadzaka zitatu ku team ya nyasa bullets pamtengo wa 5.5 million kwacha

10/01/2018

Pa 28 January Kuli masewelo apachibale pakati pa Mighty Beforward Wandares Ndi Nyasa Bullets Pa Bingu National Stadium Kupeza Ndalama Zothandizila Noma Mu Caf.

02/11/2017

Today Results
Nyasa Big Bullets 1-0 Priemer Bet Wizard
Silver Striker 1-1 Moyale Barracks

23/04/2017

TNM SUPERLEAGUE FIXTURE

06/05/2017

Kamuzu Baracks vs B4 wanderez stadium

Chitipa United vs Nyasa bullets stadium

Wizard fc vs silver strikes stadium

Dwangwa United vs Master Security

07/05/2017

Moyale vs Nyasa Bullets stadium

Blue Eagle vs Mzuni @ nankhaka

Redlions vs Blantyre United @ zomba community

@

20/04/2017

AIRTEL TOP 8 QUARTEL FINALS DRAW

Moyale vs Mafco

Kamuzu Baracks vs Blue Eaglez

Nyasa Big Bullets vs Silver Strikes

Beforward wanderez vs Azam Tigers

it's home & away

14/04/2017

Kamuzu Baracks vs Nyasa Big Bullets saturday

Mwakwela yiti pamenepa

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility?

Website