Karonga United Football Club

Karonga United Football Club

Share

you

21/01/2017

Kusatira kudwala kwa wosewera wakale wa team ya Big bullets and Dwangwa united Lunda, page ndi group lathu latengapo mbali k*tolera limodzi limodzi k*t tikam***andize pomwe pakali pano wagonekedwa pa chipatala cha kamuzu central.

Kwa omwe angafune k*thandizapo atha k*tifikira kuzera pa airtel money 0995168469, mpamba 0884443730 or National Bank acc number 3710025, kwa omwe ali kunja kwa dziko lino m***a k*tifikira pa mukuru or money gram.

Anthu okwana 27 omwe ali pama group a whatsapp apereka k54200 kufikira lero pa 21/01, tikhalebe tik*tolera mpaka sabata la mawa pa 25 January pomwe tizasakhe anthu okamuona. Ak*torera ndalama ndi Kasanga Ronard Thews.

For any queries use numbers above to call or whatsapp. Xanks in advance.

28/10/2016

Karonga United General Secretary Frank Manyazi Kalefya Banda With Beforward Wanderers Team Manager Steven Madeira At The Songwe Border In Karonga Today. Mpira Ndi Machenza.

27/10/2016

Titha Kuk*tsimikizirani Kuti Mphunzisi Wakale Wa Team Ya CIVO A "Oscar Kaunda" Kuyambira Lero Akhala Aku Phunzitsa Team Ya Karonga United Fc.. Zonsezi Apanga Ndi Ma Supporters A Team # G/s Kufc # +265996938528

15/09/2016

Team Ya Karonga United Yanyauka Ulendo Waku Blantyre Wokasewera Ndi Mateam A Wanderers Ndi Tigers. Mwa Ena Omwe Anyamuka Ndi Akulu Akulu A Team Iyi (executive) # Chairman # Vice Chairman # General Secretary/vice G/s. Team Manager And Supporters Chairman. Mtipempherere Ulendo Wabwino

05/09/2016

F.T Karonga United 3~2 Dwangwa

05/09/2016

Karonga United 3~0 Dwangwa ,,2nd Half

02/07/2016

Line up against Blue Eagles

Chimwemwe kasambara

HYGIENE mwandepeka
William gamzy
Steve msiska
Maneno nyoni

Gerald mwanza
Twisi kalolokesya
Green Msowoya
Khumbo Msowoya

Musa mwambande
Festus chikwezga

Lets support our boys 3 points loading

Photos 30/06/2016

Team ikhala ikunyamuka ulendo wolowera muchigawo chapakati komwe ikasewere ndi ma team a blue eagles en kb. Tiyeni tipereke molaro kwa anyamata athu. Ine monga ingwina yayikulu ndizakhala pano kukupasirani satane satane wa masewero loweruka en Sunday. Chofunika inu pangani invite anzanu 10

26/06/2016

FT karonga 1-0 big bullets
goal from captain hygien mwandepeka.

Congrants our boys for the first win after long starve

26/06/2016

Gooooal karonga 1 from hygien mwandepeka on 35minutes

05/06/2016

Though we lost yesterday game, lets hope en support our team on today's game will make it.

Mzuni vs ingwina

go go go boys

30/05/2016

Wednesday Mid Week Friendly March At Karonga Community Ground.

Karonga United Vs Blue Eagles

Time: 2:30pm

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Karonga?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Website

Address

Karonga

Opening Hours

Monday 07:00 - 00:00
Tuesday 07:00 - 00:00
Wednesday 07:00 - 00:00
Thursday 07:00 - 00:00
Friday 07:00 - 00:00
Saturday 07:00 - 00:00
Sunday 07:00 - 00:00