30/05/2026
Mwadzuka bwanji AGULU
Akuti Tina challenge ndinasisa kupangisa ayi ma challenge alipobe ndipo akubwera kwa amene comment yake ilwanise 70 likes π apasidwa k5000
Tiyeni kuma comment π
Arts & entertainment β
30/05/2026
Mwadzuka bwanji AGULU
Akuti Tina challenge ndinasisa kupangisa ayi ma challenge alipobe ndipo akubwera kwa amene comment yake ilwanise 70 likes π apasidwa k5000
Tiyeni kuma comment π
29/05/2026
Longtime ago with my American juice π₯€
Never give up guys anthufe tikuchokela kutali
β€οΈβ€οΈβ€οΈβ€οΈusiku Wabwino
29/05/2026
No matter how slow you go you are still ahead of those who never start β
Aguru mwaswera bwanji lero ndakutengelani ku gardens park capetown malo ooneka bwino kwambili taonelani vidio imeneyi γ #
29/05/2026
Ndikukhulupilira kuti ambiri mwalandila apa network Yathawaso kanganyase km Tizikhala nako tizigawana ndinthu ena ndimalizisa network ikagwila
ππππ
29/05/2026
Mwaswera bwanji aguru
Ndikukhulupilira kuti wina aliyese anaponya number ndalama ya mupeza tiyeni tipitilize kupanga share kuti enaso atipange follow π
28/05/2026
Mwaswera bwanji aguru apa network yagwila nkhalani okozeka tikufuna tipitilize pomwe tinalekeza Zulo thank you π
28/05/2026
Greetings from my family
How are you doing everyone wherever you are π
28/05/2026
Morning aguru
Network yah airtel ikumvutabe ikagwila muona ndikuponya ma screenshot
Zulo angoponyeledwa anthu 5 kenako network mkuyamba kumvuta mmpakana pano no service
27/05/2026
A guru muli bwanji simuti ndiutabwali Ali Koma network yah Airtel yandimvuta Lero mokuti ndangokwanisa kwaponyela Anthu 5 Onkha bansi
Ikagwila muona ikufika kwa omwe munaponya ma number letβs support each otherβs osayiwala Kupanga share like comment and invite ma friends anu kuti atijoine π
Aguru lero ndakutengelanisoni ku Simonβs town capetown malo ooneka bwino kwambili anthu omwe mwamponya ma number anu ena ndayamba kuwaponyela Koma ena sindinati malingana ndi network yandimvuta Tapangani share video imeneyi kuti tichulukane π γ