01/09/2026
Libasse Dzulo adali Man of the match mmasewero omwe Simba yawina 2_0
Libasse Gueye mwana wachabe kwambili eeeee iyeyi ndi Striker koma mmmmmm ndmwana owopsa kwambili 🤣.
🔴⚫ NYASA BIG BULLETS FANS ⚫🔴
Unofficial Fan Page | By The People, For The People 🇲🇼
Home of all The Peoples Team supporters.
Results | Lineups |Match Analysis | Fan Vibes, Live Audio Match 🔴💪
Official Page: @FCBNyasaBigBullets
01/09/2026
Libasse Dzulo adali Man of the match mmasewero omwe Simba yawina 2_0
Libasse Gueye mwana wachabe kwambili eeeee iyeyi ndi Striker koma mmmmmm ndmwana owopsa kwambili 🤣.
01/09/2026
koma Simba_yo mukuyiwona bhobho mene yachitila mma game 5 awo? 😆
no loss no draw 🙈🙈
amamayango🤭
31/08/2026
Ndangoponya popanda chifukwa 🙈
Sunday wanderers 🆚 Simba,,, CAF champions league 🤭
31/08/2026
Sama Thierry ndi player Ekhayo emwe akulandila ndalama zambili ku mighty wanderers but as of now iyeyi chibweleleni ku mighty wanderers pa season sadagolesepo zigoli zokwana 10 🤣.
Mbambande manoma inuyo nde mumatha kugula ma player akunja nziko Muno.
Kd paja mudamugula ndalama Zingati? I just want to know? 🤗
31/08/2026
David Kanyenda said.
Titenga zikho zonse chaka chino ndipo tikuyamba ndi Airtel Top 8"
Few moment later
Ekhaya 2-1 Mighty Wanderers. 🤭
Football imadana ndmatama🤣
31/08/2026
Ntchito yopulasita nyumba dzulo ku Blantyre idathera panjila chifukwa anyamata opelekela cement adakana kupitiliza ntchitoyo Pomwe adamva kuti team yawo yokondeka ya mighty wanderers idaluza ndi Ekhaya 2_1 mu finals ya Airtel top 8.🤭
Ekhaya iweyo ayi zikomo kwambili 🤣.
31/08/2026
Ukamawawona patali utha kumawona ngati ndi team km ayi ndithu Ndi lubani choir iyii. 🤭
31/08/2026
ya Mighty Wanderers Fc yawonesa chidwi chofuna kutenga mphunzitsi wakale wa timu ya Malawi komanso yemwe akuphunzitsa timu ya Master FC, .
Wanderers Fc yalengeza utsiku wapitawu kuti yamuyimisa mphunzitsi wawo wamkulu Bob Mpinganjira, kamba kosachita bwino mumpikisano wa Airtel Top 8 pomwe yagonja dzuro ndi timu ya Ekhaya FC.
Padakali pano akulu akulu a Mighty Wanderers Fc afikira aphunzitsi awiriwa omwe akuchita nawo zokambirana.
Wanderers ikuyembekezeka kukumana ndi timu ya Simba SC yaku Tanzania mumpikisano wa CAF Champions League Lamulungu likuzali pa 6 September 2026 pa bwalo lazamasewero la Bingu munzinda wa Lilongwe.
Mapalestina iwo ali chete kumwa wamkama🔴⚪️🇦🇹👊😂
⚪️🔴⚪️🔴⚪️
31/08/2026
LIONEL MESSI walengeza kuti wasiya kusewelera national yakwawo ARGENTINA.
Madalawa ntchito nde agwira ife tingoti all the Best bass🙏.
31/08/2026
Week No 15👊👊🇦🇹🇦🇹😂
Wamoto uwu Bullets Silver Strikers sopano😂👊
🇦🇹
🔴⚪️🔴⚪️