25/05/2026
coach ineyo. national team yanga ndimeneyo, always build a team around Loyd Aaron,kuno kukhala ndma player 8 otha kusinthana mpira nd azawo in tight areas like Aaron,basi tapita ka, Ena amati Aaron ndwa ma back passes,aaah inuu,mmafuna adziponya kutsogolo kuli kotseka? and it's not every ball, check his statistics muona kuti ali ndma Assist and some goals,anagoletsa akubweza kumbuyo ngati and achina amrabat nde amabwezatu kumbuyo Ngati kutsogolo mkotseka, still akusewerabe .
Iyi nd ya chachanda
25/05/2026
I still believe kuti Mike Mkwate nd key player ku FCB Nyasa Big Bullets.
Form ya Mike Mkwate,Wongani Lungu and Peter Banda this season palibe kusiyana koma kuti muone osewa akalowa, Mkwate amaoneka ofewa kwambiri pampira ndipo mafuta akanali osayamba.
Bullets yaluzapo Enerst Petro pakatipa,Gamphani of course it's okie,but inaluzaso Senaji and mfune.
ma player ndawatchulawo anali nd luso loti mpaka pano Bullets bwezi ikudalira.Ena tikakamba izi mumati player amapita kumabwera ena, yeah,ife sitikuti ma player samachoka,but sometimes ma player ena amalephera kupanga deliver ku team because of mpira omwe coach akuphuxitsa.
mpira wa Gilbert uja don't expect Peter Banda Mkwate,and Macbrams kuoneka,
ana awa amanjoya nd tiktaka football,1_21-2 basi so musaganize ngati Mkwate watha,he can deliver under π manager believe me.
look kobbie Mainoo,zinafika poti Napoli imkafuna ingopikura hence amaoneka mchabwa nthawi ya Amorim koma pano bwaa? Carrick' anangomuuza mfana menya mpira,nd uja akumenyayu, sometimes ma coach amatha kupha player.
Being a 28 year old guy it's not a problem, Mkwate akanali wamphavu,he can manage to play football in the next 7 years with the same consistency.
player akachepa mphavu osanangomutaya mwachisawawa phuziran kusunga osewera ngati mmene noma yasungira Sanudi nd Kaliat since 2013 till now π€¨
Pangani follow Page ino
Open account using promo code Abel1 Link π
https://one-vv9031.life/
Zikakuvutani kutsekula contact me on wapp
882929305
23/05/2026
7 games, under 8.5 short on target.
Booking CODE π
PqFk0ME
Register on 1WIN using promo code Abel1 Link π
https://one-vv9031.life/
Zikakuvutani kutsekula account contact me on wapp
882929305 ndikuthandizenπ€
23/05/2026
Ma goal keeper apange ma save awiri basi, kupanga save or kugwiliratu counted as a save.
Booking code π
Pq5ZO8Y
Pangani register pa 1WIN using promo code Abel1 Link π
https://one-vv9031.life/
Zikakuvutani kutsekula account contact me on wapp
0882929305
22/05/2026
No need GPS to locate where true story available π Michael Carrick is Manchester united permanent manager ππΊ
22/05/2026
PlNVaSA
Achizungulire,iyi osayerekeza kutenga βπ free advice π₯΄
20/05/2026
Week ino ndiwina bet, stay here π€²β
20/05/2026
Free advice,amene simunapange mdulidwe,khalani choncho ma guys, anthu aja amatiyitalira ku nkhondo mudzapanga regret ππ€¬π₯Ί zoopsa
20/05/2026
PbxcyTw
68 odds,9 game ticket.
Ngati smunapange register pa 1WIN mukuchedwa,uku ma option mkutapa kutaya,
Panga register pa 1WIN using promo code Abel1 Link π
https://one-vv9031.life/
Zikakuvuta kutsekula account contact me on wapp
0882929305
17/05/2026
over 0.5 card, Arsenal game,ππ€³π«³ just need single card on that game