Football Debate

Football Debate

Share

Real-time sports update

25/05/2026

coach ineyo. national team yanga ndimeneyo, always build a team around Loyd Aaron,kuno kukhala ndma player 8 otha kusinthana mpira nd azawo in tight areas like Aaron,basi tapita ka, Ena amati Aaron ndwa ma back passes,aaah inuu,mmafuna adziponya kutsogolo kuli kotseka? and it's not every ball, check his statistics muona kuti ali ndma Assist and some goals,anagoletsa akubweza kumbuyo ngati and achina amrabat nde amabwezatu kumbuyo Ngati kutsogolo mkotseka, still akusewerabe .

Iyi nd ya chachanda

25/05/2026

I still believe kuti Mike Mkwate nd key player ku FCB Nyasa Big Bullets.

Form ya Mike Mkwate,Wongani Lungu and Peter Banda this season palibe kusiyana koma kuti muone osewa akalowa, Mkwate amaoneka ofewa kwambiri pampira ndipo mafuta akanali osayamba.

Bullets yaluzapo Enerst Petro pakatipa,Gamphani of course it's okie,but inaluzaso Senaji and mfune.

ma player ndawatchulawo anali nd luso loti mpaka pano Bullets bwezi ikudalira.Ena tikakamba izi mumati player amapita kumabwera ena, yeah,ife sitikuti ma player samachoka,but sometimes ma player ena amalephera kupanga deliver ku team because of mpira omwe coach akuphuxitsa.

mpira wa Gilbert uja don't expect Peter Banda Mkwate,and Macbrams kuoneka,

ana awa amanjoya nd tiktaka football,1_21-2 basi so musaganize ngati Mkwate watha,he can deliver under πŸ†• manager believe me.

look kobbie Mainoo,zinafika poti Napoli imkafuna ingopikura hence amaoneka mchabwa nthawi ya Amorim koma pano bwaa? Carrick' anangomuuza mfana menya mpira,nd uja akumenyayu, sometimes ma coach amatha kupha player.

Being a 28 year old guy it's not a problem, Mkwate akanali wamphavu,he can manage to play football in the next 7 years with the same consistency.

player akachepa mphavu osanangomutaya mwachisawawa phuziran kusunga osewera ngati mmene noma yasungira Sanudi nd Kaliat since 2013 till now 🀨
Pangani follow Page ino

Open account using promo code Abel1 Link πŸ‘Ž
https://one-vv9031.life/

Zikakuvutani kutsekula contact me on wapp
882929305

23/05/2026

7 games, under 8.5 short on target.
Booking CODE πŸ‘Ž
PqFk0ME

Register on 1WIN using promo code Abel1 Link πŸ‘Ž
https://one-vv9031.life/

Zikakuvutani kutsekula account contact me on wapp
882929305 ndikuthandizen🀝

23/05/2026

Ma goal keeper apange ma save awiri basi, kupanga save or kugwiliratu counted as a save.

Booking code πŸ‘Ž

Pq5ZO8Y

Pangani register pa 1WIN using promo code Abel1 Link πŸ‘Ž
https://one-vv9031.life/

Zikakuvutani kutsekula account contact me on wapp
0882929305

22/05/2026

No need GPS to locate where true story available πŸ‘ Michael Carrick is Manchester united permanent manager πŸ‘‹πŸ˜Ί

22/05/2026

PlNVaSA

Achizungulire,iyi osayerekeza kutenga βœŠπŸ‘ free advice πŸ₯΄

20/05/2026

Week ino ndiwina bet, stay here πŸ€²βœ…

20/05/2026

Free advice,amene simunapange mdulidwe,khalani choncho ma guys, anthu aja amatiyitalira ku nkhondo mudzapanga regret 😭🀬πŸ₯Ί zoopsa

20/05/2026

PbxcyTw
68 odds,9 game ticket.
Ngati smunapange register pa 1WIN mukuchedwa,uku ma option mkutapa kutaya,
Panga register pa 1WIN using promo code Abel1 Link πŸ‘Ž
https://one-vv9031.life/

Zikakuvuta kutsekula account contact me on wapp
0882929305

Photos from Football Debate's post 17/05/2026

over 0.5 card, Arsenal game,πŸ‘πŸ€³πŸ«³ just need single card on that game

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Pretoria?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Address

Eike Street
Pretoria