Good evening
GoalLine Media
super league football live
Team ya Masters Security inayimitsa kaye zokambirana ndi Khuda Myaba kuti athane kaye ndi team yake yakale ya Scotland.
President wa Mighty Wanderers Thomson Mpinganjira wati ku team ya Wanderers sapanga Business yogulitsa ma players iwo amafuna ma players awo azitenga zikho. Ena anagulitsapo ma players modula koma zinawavuta mu chikho
KUSIBI KULINJI LERO PA 3 FEBRUARY 2026 NDI D7 NAMATCHENI CHITIMBE
Bob Mpinganjira wati kugonga ndi anyamata a Mzuzu City Hammers amene analimo ochepa zaonetserathu kuti anyamata ake sanasewere mpira omwr iye amayembekezera.
Tikukumana ndi team ina koma ife ndi Khumbo lathu kuti titenge chikhochi watero m'phunzitsi ongogwirizira wa Mzuzu City Hammers Lazarus Deco Nyemera.
01/02/2026
Ngati njira imodzi yofuna kulimbitsa malo ena mutimu ya FCB Nyasa Big Bullets, akulu-akulu a Mapale, alembera kalata Silver Strikers kufuna ntchito za mphangala zawo George Chikooka, MacDonald Lameck, Uchizi Vunga komanso Festus Duwe.
31/01/2026
FT | Tigers 0–2 Bullets
Maxwell Phodo (Brace) struck twice in the first half as Bullets sealed a 2–0 win and booked their place in the semifinals.
Maxwell Phodo has been voted player of the match.
Pep Guardiola manager wa team ya Manchester city mkulu uyu azagwa ndi BP taona kuzigwetsa pansi amaona ngati mpira ukupita kukalowa
Team ya FCB Nyasa Big Bullets yatsutsa kuti Mphuzitsi anamupeza kale angofuna kuphimba maso anthu potumiza ma kalata awo ofuna kulembera ntchito ngat mphuzitsi wa teamyi