05/05/2026
🚨Ochemelera timu ya Real Madrid opotsa 1 million asaina dandaulo lofuna kuti Kylian Mbappe achoke ku timu ya Real Madrid.
Ma lipoti akuti Mbappe mkhalidwe ndi lomwe lavuta pomwe akuti ananamizila kuti ndi wovulala chonsecho anapita ku zinjoyi ndi chibwenzi chake.
Kuwonjezera apo, ochemelerawa akuti, maseweredwe a Mbappe ndi zomwe ankayembekezera mwa iye sizikugwilizana.
Kylian Mbappe wachinya zigoli 85 pa masewero 100 omwe wasewera ku timu ya Real Madrid.(Innoma journalist)
05/05/2026
BREAKING NEWS!!!
Malawi’s Technical Director, Yvon Avry, has been accused of interfering with training sessions and player selection.
According to a source within FAM, Avry has been the one selecting the starting line-ups for all Malawi national teams and does not listen to coaches, sculpt platforms has learned.
05/05/2026
🗣️ Tamvaniii
📌 Malingana ndi tsamba la Bola News lati technical director yemwe bungwe la Football Association of Malawi lidamuika akuoneka kuti akumalowelera zintchito za mateam onse aziko lino makamaka pakasankhidwe ka osewera komanso kuchita zokonzekera ku mateam onse adziko lino.
Zambiri mu link iyi ⤵️
https://bolanews.co/soccer/africa/malawi-coaches-accuse-technical-director-of-interfering-with-training-selection/
#24/7
05/05/2026
"Ndi zovuta kulowa mmalo mwa Chikumbutso Salima komabe ine ngati osewera ndi chikhulupiro changa pang'ono pang'ono nditha kuzafika pa Salima " watero Clever Kalambo.
📸 FCB Nyasa Big Bullets
05/05/2026
The mocker mocked! A plastic bottle raised in April, now a mirror in May. That water must taste like bitter herbs now😁
05/05/2026
Kumaiopa nthawi inu ooh!!!🤣🤣🤣😆
05/05/2026
Mr.moyes,a little favor for Arteta.
05/05/2026
Man was carrying the “Arsenal bottle” in his pocket to show off in front of the cameras but Everton had other ideas 🤣.
05/05/2026
An Everton fan shows an Arsenal badge on his phone to the City fans 🤣
05/05/2026
🚨OFFICIAL: David Raya has claimed the Premier League Golden Glove for the 2025/26 season, his THIRD consecutive season winning the award✅
35 matches played 🧤
17 clean sheets ⛔️
05/05/2026
Mukuona kwanu Apapa akutenda Premier League ndi ndani?
05/05/2026
Mpunga wachita Chuku!!!🤣🤣🤣🤣😆