Nyasa Big Bullets The People's Team updates

Nyasa Big Bullets The People's Team updates

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Nyasa Big Bullets The People's Team updates, Sports, Blantyre.

27/04/2022

Maule Mwadzuka bwanji lero?

25/05/2020

Maule muli bwanji mutsiku larelo?

Photos from Nyasa Big Bullets The People's Team updates's post 05/04/2020

โ€ขContinue to Rest in Peace Douglas Section 65 Chirambo

โ€ขPatsiko ngati lalero lino mu mchaka cha 2015 pa 5 April ndi tsiku limene katswiri yemwe amasewera mu timu ya Big Bullets komaso Malawi the Flames Douglas Chirambo anamwalira.

โ€ขNdipo lero Douglas Chirambo wakwanitsa zaka 5 ali m'manda

โ€ขMzimu wa Douglas Chirambo upitirize kuwusa muntendere ๐Ÿ˜ญ๐Ÿ˜ข

by Dedzaboy (Siddo)

29/02/2020

Maule Musamasowe!

Lero tikupwasura timu ya Chicken Inn pa Kamuzu Stadium.

08/02/2020

!!

โ€ขLero kuli chisangalaro ku timu ya Nyasa Big Bullets pomwe katswiri mbambande watimu-yi osewera kumbuyo Charles Petro ali ndi Birthday ๐ŸŽ‚

โ€ขCharles Petro yemwe pano alimu m'dziko la Moldova kuma trials lero katswiri-yu wakwanitsa zaka 20 zakubadwa....Tiyeni timufunire zabwino katswiri-yu

๐ŸŽ‚ Hbd to you CP3 ๐ŸŽ‰๐ŸŽ‰๐ŸŽ‰...

by
Dedzaboy (Siddo)

07/12/2019

Big Bullets Fc The People's Team ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น Squad Travelling To Lilongwe ๐Ÿš๐Ÿš๐Ÿš


_Rabson Chiyenda
_Owen Chaima
____________________

Defenders
_Chirwa Gomez
_Fodya Yamikan
_Zonda Piliran
_Miracle Gabeya
_Bashir Maunde
_Nickson Nyasulu
_Charles Petro
____________________

_*Midfielders
_Chimango Kaila ยฉ_
_Fisher Kondowe
_Henly Kabichi
_Nelson Kangunje
_Righteous Banda
_Ben Manyozo
_Precious Phiri
_Dalitso Sailes
_Chimwemwe Idana
_Mike Mkwate
_Peter Banda
___________________


_Chiukepo Msowoya
_Bright Muthali
_Hassan Kajoke
_Luke Chima
_Patrick Phiri
____________________

Panel
_Kalisto Pasuwa
_Heston Muthali
_Swadick Sanudi
_James Chirapondwa
_Malumbo Chikoko
_Felix Mwalule
_Kimpho Loka


_John Kintu Lanjes
_Precious Sambani
_Ernest Kakhobwe
_Sakhani Mkandawire

The team has just left Blantyre to Lilongwe ๐Ÿš๐Ÿš๐Ÿš
_____________________

Mukawelenga muzitumiza kuma group ena kuti athu ena ajoyine nawo group ino plz

Zeni-zeni

by
โœ Dedzaboy (Siddo )

20/11/2019

Nyasa Big Bullets Fc The People's Team ๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น๐Ÿ‡ฆ๐Ÿ‡น Today's Training Update @ Blantyre Sports Club โšฝ๐Ÿƒ๐Ÿป


_Ernest Kakhobwe
_Rabson Chiyenda
____________________


_Sakhani Mkandawire
_Yamikan Fodya
_Piliran Zonda
_Miracle Gabeya
_Bashir Maunde
_Gomez Chirwa
_Nickson Nyasulu
_Charles Petro
____________________


_Chimango Kaila ยฉ
_Fisher Kondowe
_Henly Kabichi
_Nelson Kangunje
_Righteous Banda
_Ben Manyozo
_Macpharlen Ngwira
_Dalitso Sailes
_Chimwemwe Idana
_Mike Mkwate
_Peter Banda
_Ernest Petro
____________________


_Chiukepo Msowoya
_Bright Muthali
_Hassan Kajoke
_Luke Chima
_Patrick Phiri
_____________________

Panel
_Kalisto Pasuwa
_Heston Muthali
_Swadick Sanudi
_James Chirapondwa
_Malumbo Chikoko
_Kimpho Loka
_Felix Mwalule
____________________

Flames U-20 Camp
_Elias Miss
_Mwakifuna Aziz
_Peter Mponda /Coach


_John Lanjes
_Pre Sambani
_Precious Phiri
____________________

โ€ขโ€ขPrecious Phiri* sanapange nawo * training lero kamba kakuti dzulo walumidwa ndi *njoka* komano osakhala ndi khawa kweni-kweni *Precious Phiri* akhala akubwelera pa ground chapompano koma *tingomufunira* kuchila mwq msanga ๐Ÿ™ star wathu-yu.

Musaiwale kupanga forward kuti ena athe kuti joina group ino
____________________

Zeni-zeni

Team Nyasa โˆšโšฝ๐Ÿƒ๐Ÿป
Mighty Tigers Samala??

by Bullets Diehard
Dedzaboy (Siddoo)

17/11/2019

Page ino yapangidwa kumene guyz ndiye chofunika mukawelenga muzitumiza kuma group ena kuti athu ena athe kuti joina

๐Ÿ”ฅโค๐Ÿ’ช

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Blantyre?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Telephone

Website

Address


Blantyre