Bawo Pa Malawi

Bawo Pa Malawi

Share

Kulemekeza chikhalidwe kuyambile pa chidwi chathu pamasewero a Bawo.

04/01/2024

Koma Bawo osaiwalatu kaamba ka holiday imeneyi

20/07/2023

Mwadzuka Bwanji A Malawi.

15/07/2023

Iyi ndi Kameza Round-About Bawo Club. Akufuna aipange challenge ndindani tikaone katakwe kunkhani yotakata .

14/07/2023

Mwadzuka bwanji a Malawi. Kwazizilatu, yemwe akufuna bawo tiyakhulane.

12/07/2023

Ngati mukufuna kudziwa zambili zokhuzana ndi masewero a Bawo komanso omwe amayendesa masewelowa muno Malawi. Chonde Yankhulanani ndi awa;

Chairman Mr Banda: +265 992 50 14 06
Vice Chair Mr Alick: +265 993 63 31 12
Secretary Mr Frank:
+265 888 57 35 70

12/07/2023

NTHAWI YAKWANA. AKATSWILI ODZIWA BAWO ADZIWIKE PANO PA MALAWI.

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Blantyre?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Website

Address


Blantyre