09/11/2023
BOLA Kunthazi
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from BOLA Kunthazi, Sports, Blantyre.
09/11/2023
04/11/2023
Ovota alangazidwa kudzavota mwa nzeru pa zisankho za mtsogoleri wa bungwe pa Football Association of Malawi FAM
04/11/2023
Mighty Mukuru Wanderers FC MIGHTY MUKURU WANDERERS
01/11/2023
President wa timu ya Mighty Mukuru Wanderers FC wapempha ochemelera kuti adzafike mwa unyinji Sunday limeneli pa Kamuzu stadium pomwe MIGHTY MUKURU WANDERERS ikadzasewere ndi FCB Nyasa Big Bulletss
31/10/2023
Balawala Vingula wakhala munthu oyamba kubwera poyera kulengeza kuti apikisana ndi a Nyamilandu.
By Charles Chataza BOLA Kunthazi
31/10/2023
Facebook Lite for Android This version of Facebook uses less data and works in all network conditions.
31/10/2023
Ofesi ya mulembi wamkulu Ku bungwe la Football Association of Malawi yatulutsa dongosolo ya momwe zinthu zitayendele
By Charles Chataza
BOLA Kunthazi
Pali anthu ochuluka omwe aonetsa chidwi chopikisana ndi mtsogoleri wa bungwe loyendetsa masewero a mpira wa miyendo mdziko muno la FAM. BOLA Kunthazi ikuuzani zambiri posachedwapa.
Mphunzitsi watimu ya FCB Nyasa Big bullets Calisto Pasuwa wadandaula ndi mmene akuluakulu oyendetsa mpira ku Malawi amaikira masewero a mipikisano mdziko muno.
Passuwa walankhula izi pakutha pa masewero omwe timu yake inagonjetsa timu ya Kamuzu Barracks 3-2 mu TNN super league lachitatu pa bwalo la Kamuzu mu mzinda wa Blantyre.
Malingana ndi Pasuwa izi zimachititsa kuti adzitha mphamvu mofulumira zomwe sizingapindulire timu ya dziko lino ya Flames.
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Website
Address
Blantyre