Nyong'o mwandire

Nyong'o mwandire

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Nyong'o mwandire, Sport & recreation, Sorgin box 2, Blantyre.

14/07/2025

#

Ilyas Abdul Karim, phungu wadera la kumwera kwa boma la Chikwawa waulura kuti ayima payekha pachisankho chikudzachi.

Iye anali wa chipani cha Malawi Congress MCP.

Ndipo waulura izi lero pa Ngabu pomwe Pali mafumu ndi anthu osiyananasiyana

22/02/2024

Osewera atatu lanjes nkhoma maxwell gasten phodo goalkeeper Christopher mikuwa wa mafco ndi omwe akhare akulimbilina mphondo ya osewera omwe asewera bwino airtel top 8 season ya 2023 nkhoma ngat top goal score komanso phodo ngat puliya amene wasewera magemu awiri ndikugolesa zigoli ziwili pamene Christopher mikuwa ngat otchinga pagolo wapamwamba

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Blantyre?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Culinary Team

Attire

Website

Address


Sorgin Box 2
Blantyre