06/06/2026
Zathela mofananitsa Mphamvu
To discuss all the issues concerning sports updates and info of local sports and international.
06/06/2026
Zathela mofananitsa Mphamvu
05/06/2026
MPHATSO SITIMADELELA
Bungwe loyendetsa Mpira kuno ku mudzi la FAM lalandila mipila yogwilitsidwa kale ntchito (second hand balls) yokwana 36 Kuchokela ku Japan Football Association
Izi zithandizila kuti ubale pakati pa maiko awili wa ukule komaso tizithandizana muzambiri
02/06/2026
Ma Club enawa atangoti azichepesa kuchilemba ntchito ichichi Ma Timu anuwa adzukatu
Even upangili okha akhoza kukupasanitu
2026 season Mpira wayaka
Uthenga sulemela ndipo umveke muliko
Aaah Za satanic zo
18/05/2026
Timu ya Ndirande Stars yalowa mu Mgwilizano ndi kampani ya Sharma Electrical lero
Iwowa apaleka uniform za ndalama yokwana 15 million kwacha ndipo ati pakadutsa miyezi isanu ndi umodzi agula bus yoti timuyi izigwilitsa ntchito
Nathan Sharma kuchokela ku Kampaniyi wati malingalilo otengelatu timuyi kukhala yawo alipo ndipo zonse akukambilana ndi amtsogori a Ndirande Stars
Ndirande Stars ikusewera mu mipikisano wa NBS National Division League pomwe masewero awo oyamba afananitsa mphamvu ndi FOMO FC pa bwalo la Mulanje
18/05/2026
It's too early
Ma coach athotholedwa season ino
17/05/2026
Final results ya National Division League
Ma Timu atolela ma points motere
14/05/2026
Chi League cha Nyatwa ichi
Weekend imeneyo maswero alipo motere, ulendo otaya ndi kutolela ma points mu NDL wayambika
Adutse ndani apa
10/05/2026
😜 My fellow football lovers
Malingana ndi mmene zakhalila ndi west ham, ife timati tilengeze kuti chinthuchi chapita basi moti atsogola kwambili moti sangapezekenso
Ndi mau amenewa tiyeni tiwafunile zabwino ma gunners
| Monday | 09:00 - 17:00 |
| Friday | 09:00 - 17:00 |