Grandmax Sports Updates

Grandmax Sports Updates

Share

Sports and Recreations

-Sports News Coverage
-Live Football Commentary.

03/06/2026

Line up For Scorchers Against Tanzania πŸ‡ΉπŸ‡Ώ This Afternoon...


03/06/2026

Wa lero !!!!


03/06/2026

Masapota a CRECK Sporting Club Sim'mene anayakira moto, Vichewa Vamthunzu mkati.

Mmmmmm bwanji Zambiri muzimvere nokha ine ndingayambe kuonjezera.


03/06/2026

NKHANI YOMVETSA CHISONI! πŸ•ŠοΈπŸ•ŠοΈπŸ•ŠοΈπŸ•ŠοΈπŸ•ŠοΈ

Northern Region Football Association ikulengeza za imfa ya Thoko Mkandawire yemwe anali modzi mwa akulu-akuku owowo za chitetezo mchigawo chi (Steward) omwe amwalira dzulo pa 02 June 2026 pa chipatala cha Mzuzu Central Hospital.

Ndipo mwambo oyika m'manda thupi, uchitika kumudzi kwa ku Zolozolo..

Mzimu wawo Uwutse muntendele πŸ•ŠοΈ πŸ•ŠοΈ


03/06/2026

Zonse zokonzekera kukhadzikitsa kwa ligi ya mchigawo chakummawa ya Eastern Region Football Association - Let them play zili mchimake tsopano.

Malinga ndi mlembi wamkulu wa bungweli Elia canton Nyirongo wati zonse zikuyambika Loweruka lino pa bwalo la Vision Ku Ntaja m'boma la Machinga pamene ma timu a Ntaja Rangers komanso Nselema United akhale ikufwafwanthana pa tsikuli.

Ligi ya mchigawochi imathandizidwa ndi kampani ya H Adams pansi pa Durata Batteries.


02/06/2026

AndrΓ© Onana 𝐑𝐄𝐓𝐔𝐑𝐍𝐒 to Man United and he’s set to join 𝐏𝐑𝐄 π’π„π€π’πŽπ under Carrick

Trabzonspor remain interested in the goalkeeper after loan, negotiations will follow this month to try agree new deal πŸ‘€

The possibilities of staying at Man United are slim β€” with the Turkish side π“π«πšπ›π³π¨π§π¬π©π¨π« 𝐬𝐭𝐒π₯π₯ 𝐑𝐨𝐩𝐒𝐧𝐠 𝐟𝐨𝐫 𝐚𝐧𝐨𝐭𝐑𝐞𝐫 π₯𝐨𝐚𝐧 move.

Source: Fabrizio Romano


Photos from Grandmax Sports Updates's post 02/06/2026

The Scorchers welcomed back Faith Chinzimu following her historic achievement of becoming the first Malawian footballer to win a UEFA Women's Europa Cup title with BK HΓ€cken FC.


02/06/2026

SRFA FINCA Division League Week 2 Fixtures

Saturday, 6th June 2026

7.Ekhaya Reserve v Liberty Fc@Mpira 2.30pm
8.The Boyz v Zingwangwa United 2.30pm
9.Chiradzulu United v Nyambadwe United Ground 2.30pm
10.FCB Nyasa BB Reserve v Mwanza United Stadium 2.30pm

Sunday, 7th June 2026

11.Nchima United v Wanderers Reserve 2.30pm
12.QPL All Stars v Mwanza Stars 2.30pm
13.Fc Thondwe v Ntopwa Fc@Mpira Stadium 2.30pm



02/06/2026

Mizwanya kuuzaana Zochita....


02/06/2026

Chisomo Nkhoma wasankhidwa kukhala mphunzitsi ongogwilizira wa timu ya CRECK Sporting Club .


Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Blantyre?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Telephone

Address


Blantyre