UKALI WANU

UKALI WANU

Share

Ufulu wanga

03/06/2023

Good morning kulikonse komwe muli
Tsopano tiyamba kukupatsa nkhani mwakathithi zomwe zizingochitika kumene

07/09/2022

Simba vs NBB
What's your prediction?

Profile pictures 07/05/2022

MPHEKESERA!
Atachotsedwa ntchito yophunzitsa timu ya fuko la dziko ya Malawi the FLAMES ndi bungwe loyendesa masewero mdziko muno la Football Association of Malawi (FAM), Meck Mwase atha kulowera ku timu ya Mighty Mukuru Wanderers ngati mphunzitsi wamkulu (head coach) watimuyi!

Mukuona ngati kubwera kwa bambo Mwase ku Manoma zitha kusintha zinthu?

05/05/2022

Tadzu sitiziwa kumeneko?🙏

17/03/2022
07/12/2021

Mukuganiza kuti palakwika ndi pati pa squrd yomwe atulutsa

03/12/2021

Mawa live pa kamuzu stadium pa Blanryre darby 👉🏻🏃

ADM jame ali konko

28/11/2021

Nchifukwa chiyan ambuye amatikonda? 🙏

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Chikwawa?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Telephone

Website

Address


Chikwawa
4242