FT : SILVER 1:0 BULLETS. KAONGA CHAWA PA 68 MINUTES
Silver FC
To share news about our team
Silver strikers reserve are the champion of nyasa finance after beating kamuzu barracks 6:2 . Ma bankers ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ
We are now into finals after beating civo 2:0. Next it's Bullets .who will be the champion?
Tiyeni tiyeni mawa tikachemerer team yanthu pomwe ikankhale ikuthambitsa civo pa Bingu . Ma banker ๐ฅ๐ฅ๐ฅ๐ฅ kuti BUUUUUUUUยก!!!!!
Koma chi team ichi ndi mbambande. ๐ฅ ๐ฅ ๐ฅ ๐ฅ
Mwamvota kale? SST to 3039
Send an SMS to 3039 to vote for the player of season. For us just write ss t to that number. Only once. Tiyeni timumvotere Blessings Tembo
Up to this time, silver has pocketed 33.5 million. 25 from FDH, 7.5 for being run-up in tnm and 1 for being finished position 1first round of tnm. ๐ฅ ๐ฅ ๐ฅ ma ๐ฆ
Muhamad Sulumba yemwe adasewerapo wanderers komanso bullets, akuyensa mwai ku team ya silver pamodzi ndi silver chawe komanso mmodzi ochokera ku karonga.
Ma team Ena ndiye akugula ma player koma ife kuli ziiii ngakhale tsogolo la ma coach anthu silikudziwika. Ndiye ma supporter akupepha Rodrick Gonani kuti ayambitse zikozekera.
Young chimodzi Jr wasaina contract ina us zaka zitatu ndi silver
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Kapiri
Lilongwe Area 15
LL