Ndeleman Haward

Ndeleman Haward

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Ndeleman Haward, Sports Event, Magada School, P. O. Box 118, Namitete, Lilongwe.

16/08/2023

Congratulations to both PSLCE and JCE students who have passed their exams. To those who failed to make it don't give it's not the end of your future, start it again and surely you'll really do better.

03/03/2022

There is nothing impossible in life unless you fail to work extra hard and stop trying

Photos from Ndeleman Haward's post 19/07/2021

Let's us be what we can be

22/04/2021

LET EVERY BE WHAT HE /SHE CAN BE

26/07/2020

Pomwe a Malawi ambiri akuyembekezera mwachidwi k*ti aone kusintha komwe atsogoleri adziko lino adalonjeza.Zadziwika k*ti pali kugawikana paka pa anthu m'dziko muno pomwe ena akuonetsa kokondwa ndi ganizo komanso speech yomwe mtsogoleri Wa dziko lino adalankhula k*ti onse amene adaba ndalama za boma mu ulamulilo omwe wapitawu sakhululukiridwa koma k*ti akumana ndi lamulo lomwe ligwire ntchito pa Iwo koma izi Sizidasangalatse ka gulu kena ka anthu. Mwachitsanzo mneneri Wa chipani cha DDP a Nicholas Dausi adatanthauzira Kumangadwi kwa anthuwa k*ti ndi witch hunting kapena k*ti akumangidwa kamba ka ndale chabe ati pofuna kufooketsa chipani chawo.

Achinyamata ambiri akhumudwa ndikukhala chete kwa boma posalankhulapo chilichonse chokhudza kuyambanso kwa sukulu mdziko muno.Iwo apempha mbali zonse zokhudzidwa k*t i zilowelerepo kaamba kak*ti achinyamatawa akukumana ndimavuto ochuluka komanso kuchitiridwa nkhanza zosiyanasiyanamadera mwawo chitsekereni cha sukulu mdziko lino m'mwezi Wa March chaka chino.

26/07/2020

Pomwe a Malawi ambiri akuybekezera mwachidwi k*ti a one kusintha komwe atsogoleri adziko lino adalonjeza.Zadziwika k*ti pali kugawikana paka pa anthu m'dziko muno pomwe ena akuonetsa kokondwa ndi ganizo komanso speech yomwe mtsogoleri Wa dziko lino adalankhula k*ti one amend Adana ndalama za boma my ulamulilo omwe wapitawu sakhululukiridwa koma k*ti akumana ndi lamulo lomwe ligwire ntchito pa Iwo koma izi Suzuki sang slats a ka gulu kena LA anthu. Mwachitsanzo mneneri Wa chipani cha DDP a Nicholas Dausi adatanthauzira Kumangadwi kwa anthuwa k*ti ndi witch hunting kapena k*ti akumangidwa lamba ka ndale chabe at I pofuna kufooketsa chipani chawo.

Achinyamata ambiri akhumudwa ndikukhala chete kwa boma posalankhulapo chilichonse chokhudza kuyambanso kwa sukulu mdziko muno.Iwo apempha mbali zonse zokhudzidwa k*t i zilowelerepo kaamba kak*ti achinyamatawa akukumana ndimavuto ochuluka komanso kuchitiridwa nkhanza zosiyanasiyanamadera mwawo chitsekereni cha sukulu mdziko lino m'mwezezi Wa March chaka chino.

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Lilongwe?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Website

Address


Magada School, P. O. Box 118, Namitete
Lilongwe
1998