06/07/2026
🚨 Karonga United yalengeza kuti wayimitsa pa ntchito mphunzitsi wao wamkulu Audrow Makonyola kwa masewero atatu kutsatira kusachita bwino kwa timuyi mu ligi ya FDH pomwe angokwanitsa kupambana kawiri, kugonja kanayi ndi kufananitsa mphamvu katatu m'masewero 9.
Timuyi yomwe ili pa nambala 13 pakadali pano inagonja 3-1 ndi timu ya GC Dedza Dynamos m'masewero aposachedwa.
Chris Crespo Chinkwita ndi yemwe wapatsidwa ntchito yogwirizira.
Wolemba : Jamie Michael
GBS TV sports desk
06/07/2026
Portugal And Spain Line Ups ⚽🔥
Inu Mwakwera iti⁉️
04/07/2026
Half Time Results
Big Bullets 1-0 Creck SC
Karonga 1-2 Dedza dynamos
Blue Eagles 1-0 Moyale
03/07/2026
🔵 Manoma akuti nthawi yovulaza ma timu yakwana pomwe Lameck Mithi wayamba zokonzekera kuchokera kovulala
GBS TV sports desk
03/07/2026
🚨 Ma Banker Adakali pamwamba kungositana 1 point ndi Blue Eagles komanso Bullets.
GBS TV sports desk
03/07/2026
🗣️ “Cape Verde will eliminate Lionel Messi’s Argentina.” 🇨🇻🇦🇷
🔮😳 The “juju” strikes again⁉️
Ghanaian spiritualist Nana Kwaku Bonsam has caught the football world’s attention after correctly predicting the exits of Ivory Coast and DR Congo at the World Cup. 👀
Now he’s made his boldest prediction yet…
🗣️ “Cape Verde will eliminate Lionel Messi’s Argentina.” 🇨🇻🇦🇷
Can Cape Verde pull off one of the greatest upsets in World Cup history, or will Messi prove the prediction wrong⁉️⚽
GBS TV sports desk
03/07/2026
Sergio Agüero was asked which strikers he believes were better than him.
❌ Gonzalo Higuaín? - "No."
✅ Carlos Tévez? - "Yes."
❌ Edinson Cavani? - "No."
✅ Luis Suárez - "Yes."
❌ Fernando Torres - "No."
❌ Radamel Falcao - "No."
❌ Erling Haaland - "No."
✅ Karim Benzema - "Yes."
❌ David Villa - "No."
❌ Gabriel Jesus - "No."
❌ Robert Lewandowski - "No."
GBS TV sports desk
03/07/2026
🚨Mphunzitsi wa Bullets Wedson Nyirenda wadandaula ndi chiganizo chomwe Babatunde wapanga posankha kupita ku Costa do sol ya ku Mozambique m'malo mwa Bullets. Wed wati amakhulupilira kuti zi ntchito za Baba zikanatha kutengera Maule mlingo wina akabweleranso ku Bullets.
Babatunde wapita ulele ku Costa do Sol kutsatira kutha kwa mgwirizano wake ku Venda FC.
GBS TV sports desk
03/07/2026
🏁 FIFA World Cup 2026
✅ Full Time Results
🇪🇸 Spain 3-0 Austria 🇦🇹
✅ Spain advance to the Round of 16.
🇵🇹 Portugal 2-1 Croatia 🇭🇷
✅ Portugal advance to the Round of 16.
🔥 Spain and Portugal book their place in the Round of 16!
GBS TV sports desk