23/07/2026
Pig Finisher Premix
Uyu ndi premix amene timagwiritsa ntchito Popanga chakudya chankhumba kuti zinenepe mwachangu ndikugulisidwa ngati nyama.
ZIWETO ENTERPRISE is a network of franchised agro/vet shops providing veterinary solutions for small
Ziweto is a pioneering company building a unique national network of branded retail outlets (6 to date) selling quality livestock inputs, services and training to livestock farmers across Malawi.
23/07/2026
Pig Finisher Premix
Uyu ndi premix amene timagwiritsa ntchito Popanga chakudya chankhumba kuti zinenepe mwachangu ndikugulisidwa ngati nyama.
Pig Sow and Weaner Premix
Kwa alimi omwe mumapanga nokha chakudya cha Nkhumba, Ku Ziweto Agrovet Shops tili ndi Pig Sow and Weaner Premix amene ali ndi michele yofunikila kwambili ku thanzi la Nkhumba. Pig sow and weaner amathandiza kuti mayi wa Nkhumba akhale ndikuthekela kobeleka ana ambiri komanso kuti ana akasiya kuyamwa akule ndi thanzi.
Ziweto Enterprises Limited ZIWETO ENTERPRISE is a network of franchised agro/vet shops providing veterinary solutions for small
16/07/2026
Thank you, Kwithu farms, for trusting Ziweto Enterprises. We're proud to support your success with quality veterinary solutions and technical expertise. Together, we're raising the value of livestock.
Ziweto Enterprises Limited visited our farm the other day🙏🏼
Grateful 🙏🏼
13/07/2026
Vita Boost ndi ma Vitamini omwe amathandiza Nkhuku zanu kuti zikule bwino komanso kukhala ndi nthanzi. Vita Boost timapeleka kwa Nkhuku za mtundu wina uliwonse.
Vita Boost akupezeka muma shop onse a Ziweto Agrovet muno Malawi.
Quality feed. Better performance. Greater profits.
Give your livestock the nutrition they deserve with premium Ziweto Feeds. Our updated prices are now effective 9 July 2026. Visit your nearest Ziweto Agrovet Shop or contact our sales team to place your order today.
Ziweto Enterprise – Raising the Value of Livestock for Better Human Lives.
Ziweto Enterprises Limited ZIWETO ENTERPRISE is a network of franchised agro/vet shops providing veterinary solutions for small
09/07/2026
Nthawi yodandawula kuti nkhuku zanu zikuyikila mazira ang'ono ang'ono ndi mbiri yakale, alimi a Nkhuku za mazila otsogola akugwiritsa ntchito Layer Extra omwe ndima vitamin ofunikila ku Nkhuku za mazira, Layers Extra amathandiza kuti nkhuku ziziyikila mazira akuluakulu komanso olimba chikopa.
Layers Extra akupezeka muma shop onse a Ziweto Agrovet muno Malawi.
07/07/2026
Broiler Booster ndima vitamini ofunikira kwambiri ku Nkhuku za nyama kuti zikule msanga komanso ndi thanzi. Amathandiza kulimbitsa mafupa, kuwonjezera minofu, komanso kulimbikitsa chitetezo cha mthupi kuti nkhuku zisadwale matenda osiyana siyana.
Broiler Booster akupezeka ma shop onse a Ziweto Agrovet muno Malawi.
04/07/2026
Dear Valued Customers,
Kindly note our operating schedule for the weekend and Monday, 6 July.
02/07/2026
Chick Start ndi ma Vitamin ofunikira kwambiri kwa anapiye kuti akule mwa thanzi. Amathandiza kupereka mphamvu, komanso chikhumbo khumbo chofuna kudya ndi kumwa madzi.
Chick Start timapereka kwa anapiye a nkhuku zonse.
Tetezani Nkhuku zanu ku matenda osiyanasiyana monga Chitopa, Nthomba ndi ena potsatira ndondomeka za katemela moyenela.
Ziweto Enterprises Limited ZIWETO ENTERPRISE is a network of franchised agro/vet shops providing veterinary solutions for small
| Monday | 08:00 - 17:00 |
| Tuesday | 08:00 - 17:00 |
| Wednesday | 08:00 - 17:00 |
| Thursday | 08:00 - 17:00 |
| Friday | 08:00 - 17:00 |
| Saturday | 08:00 - 14:00 |