26/02/2024
Zochitika pa dziko
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Rab Mag Hucker, Sport & recreation, Lilongwe.
26/02/2024
Zochitika pa dziko
10/11/2023
Guys please i want 500k followers
09/11/2023
Mauleeeeee
Moooooooo
Fireeeeeeee
17/09/2023
Nonse amene mukuyidziwa film iyi,mulibwanji?
Thupi katswiri osewera mpira Thuso Paipi,liyikidwa m'manda lero muzinda wa Blantyre..
Nzimu wake uwuse m'ntendere.
08/09/2023
Ifa ya amene anali katswiri wamasewero a mpira wa miyendo,Thuso Paipi, yakhumudwitsa fuko lose la Malawi 🇲🇼 ndipo tili muchisoni.Thuso Paipi,anachokera ku team ya Sure stream Academy,asanapite ku team ya Silver Strikers.
Mzimu wake uwuse mu ntendere..
The biggest Radio station
1.MBC🇲🇼
2.ZBC🇲🇼
3.TIMES🇲🇼
4.TIMVENI🇲🇼
5.ISLAM🇲🇼
Below 5k followers
Promot their pages here
23/08/2023
Pankhani ya music M'malawi muno komaso ndi mayiko ena akunja,sitingakambe za luso la anthu oyimba,osantchulako Physix..
Uyuyu ndi dolo kwambiri,ulemu upite koyenera kupita ulemu.
But for me having a chance to choose one of top 10 artist,can choose Man Phyzo....
Big up to you Physix, continue to give us a good songs..