Morning Bankers?
Ma Bankers Tinyamuladi Super League,
Sports Proglam only
Koma mwati ndinu Supoterd wa The Centro Bankers?tatchulan dzina la pleyer wakale ine ndawambapo Dave Moya nanga inu?
Mwadzuka bwanji abale anzanga mmawa wa lelo pa 01/03/2019.
Ndilandileniso ndinkhani zamasewelo koma mosataya nthawi tiyambe motele.
Masapota okwiya a Silver Strikers aopseza akuluakulu k*t asayekeze kumusainitsa contract katswili wakale wa B United,,Noma komanso B Bullets Muhammad Sulumba kaamba kuk*t pleyer yu ndiwankulu komaso perfomance yake ndiyotsika potengela ndimmene amasewelela kale k*t komanso ku Silver Strikers sikothela. Sulumba yemwe wakhala akuyesa mwayi kwa sabata ziwili koma zotsatila zonse zidziwika sabata yamawa,,,,,mafuso nkumat atengedwe kapena ai?
Nkhani ina ndiyak*t mphuzitsi wankulu wa Silver Strikers Yougoh Chimodzi jr wasankha Hellings Mwakasangula kukhala Team Manager wa Silver Strikers ndie mwamulandila?,,,,tiyeni tisiyane p***a
-George-Kaudzu
Mwaswela bwanji okondedwa anzanga madzulo alelo pa 27/02/2019 kulikonse komwe muli?
Ndimanena zija k*t mfana uja after training zatheka ndi contract ya zaka zitatu.
wanuo
SHERIF SHAMAMA
MUHAMMAD SULUMBA
RAFIC M***A
Manong'onong'o zikuonetsa ngat Sherrif atha kusaina after training
Zongotipeza kumene.
Dzulo Blessings Tembo Teacher wapanga nao training koma sanasaine
-Kaudzu
THE BANKERS TINYAMULAD SUPER LEAGUE is a group of Silver Strikers fc fanatics who are dedicated to their team in any means, Whether finacially or in Supporting members are encourage to give MORALE to their team, and post their comments here to way they went their team to improve
-KAUDZU-wanu-wanu
Mwaswera bwanji ma anzanga masana alelo pa 26/02/2019.
Mosataya nthawi tingodziwitsana mwapadeladela.
SUPPORTERS COMMITTEE
ikuitanitsa masapota tomse k*t tikumane ndi main Executive imene yasankhidwa kumene,,,,after training ndie mwakonzeka?
Pomwe dzulo tayamba ma training athu ndipo chilichose chili mchimake,,,,tikayake moto basi
NEWS FROM SILVER STRIKERS EXECUTIVE
Chair -Pater Chando
Vice -Slick Tahuna
Sec- Laurence Gone
Vice -Innocent Kadammanja
Treasurer+Judith Kachimanga
Vice-Patrick Mbiliyakula
Committed Members;
Atom Kamtepa
Davide Daimon
Dr Lameck Chinula
Getrude Moses
One Wankulu Wankulu admin George. Kaudzu, ,,,,,,,,,,,,,
20/02/2019
Mwadzuka bwanji ma Banker anzanga kulikonse komwe muli? Tatengatu M Sulumba inu maganizo anu ndiotan negati oyikonda Silver Strikers?
Mark Fodya wasainaso contract ina ndi Silver Strikers.
kotero amene amafuna osewerayu akayang'ane kwina
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Website
Address
Lilongwe