Chanco Socialz

Chanco Socialz

Share

Promoting social capital, interaction and bonding through soccer ⚽⚽.

01/01/2026

Happy New Year a Chanco!!!
Chaka chino tiwina zonse, mpira, mmoyo ndi ma banja!

28/12/2025

Koma Jubeki!!!

28/12/2025

A Jubeki ndi Major komupelekeza Gwamba......

Photos from Chanco Socialz's post 28/12/2025

Iih koma ukwati wa Gwamba tinanjoya😂....

Tiziponya content pamene tili mkati mosankha tcheya wina oyendetsa dongosolo la kireti.

12/11/2025

Congratulations to our Admin Raster man Clovix

08/11/2025

Honorable Silvester Ayuba James popita mutitenge..... Komanso team ikusowekera Pepe iyi.....

08/11/2025

Introducing Master Jubeki......

"Umatiuza tizimwa mowa iwe ukumapita ku school ku Zambia....."

Mukakumana naye muwuzeni agule kireti.

07/11/2025

Mawa tikupatsirani Master Jubeki. Congratulations Hardy Zizou Jubeki

Dolo👍🏾

26/10/2025

Tangoyika opanda chifukwa, muoneniko Jubeki aka a Eight.....

26/10/2025

Ichi nde Sokoneza ilibe nacho mawu, ichichi ndichiballer mpaka Manyozo Jr kuthawa kukamenya ku 2😂......

25/10/2025

Full time
Chanco Socialz 2
Sokoneza 1

Tawafinya.....

25/10/2025

Tawachapatu....

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Lilongwe?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Website

Address


Lilongwe