voti yanga ine๐โโ๏ธ
George fuu
Social life, simple
23/08/2025
Kuzizira kochimwitsa๐คฆโโ๏ธ
Vinako
Komaso Zeze simungamupange compare ndi mwana okuti or pa JETU sanafike umenewo nde timati ugong'oli
Zeze Kingston kumalawi kuno ali mu level yayekha mu amapiano muja
Osamaphatikiza ana oti anakanunkha mkaka wamabere ndi Legend
pano olo mkodzo wakhoma lakubafa woti mbuzi inyambite ukusowa ๐ kwaipa ๐๐๐
26/09/2024
Akamati chida chabambo amanena chimenechi
24/09/2024
Basitu malinga ndikutenthaku Gee washevedwa kale
"Akuti mmandamo zukani mupange unfollow. Ma foni aikidwa pa office ya a DC."
23/09/2024
Ma driver osathawira pa window ku school ya driving amachita kuziwiratu kuti this sign post imatanthauza ku mwayandikira kufika pa msundwe osatulusa mutu pa window
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Website
Address
Lilongwe