03/06/2026
FULL TIME ⚽
🇱🇺Luxembourg 0-1 Italy🇮🇹
FOLLOW Mtonda Land Consultancy
OFFICIAL Page Created for Sports Analysis, Sports Updates & Sports Podcasts Globally.
03/06/2026
FULL TIME ⚽
🇱🇺Luxembourg 0-1 Italy🇮🇹
FOLLOW Mtonda Land Consultancy
03/06/2026
FULL TIME ⚽
🇵🇱 Poland 2-2 Nigeria🇳🇬
FOLLOW Mtonda Land Consultancy
03/06/2026
FULL TIME ⚽
🇳🇱Netherlands 0-1 Algeria🇩🇿
FOLLOW Mtonda Land Consultancy
03/06/2026
FULL TIME ⚽
🇦🇱 Albania 0-1 Israel 🇮🇱
Follow Mtonda Land Consultancy
03/06/2026
FULL TIME ⚽
🇨🇩DR Congo 0-0 Denmark🇩🇰
FOLLOW Mtonda Land Consultancy
03/06/2026
FULL TIME ⚽
🇬🇮GIBRALTAR 4-0 BRITISH VIRGIN ISLANDS 🇻🇬
Mtonda Land Consultancy
03/06/2026
Zigawenga za timu ya Dziko la Malawi zapanga zokozekera zawo zomaliza pomwe mawa akuyembekezeka kunyamuka kupita ku Ethiopia mu mzinda wa Diredawa komwe akukapimana mphavu ndi Timu ya Dzikolo loweruka ndi lachiwili likubwerali.
Follow Mtonda Land Consultancy
03/06/2026
Timu ya Ethiopia yapanga zokozekera zawo zomaliza in Addis Ababa lero pomwe mawa ikuyembekezeka kupita ku Diredawa komwe AKAKWAPULANE modetsa nkhawa ndi Timu ya Malawi the Flames loweruka komaso lachiwili
Follow Mtonda Land Consultancy
03/06/2026
Ma Strikers ena Mulungu adawayendera nyengo zawo ndithudi 😀
BABATUNDE ADEPOJU wa VENDA FC pa magemu 16 omwe Timuyi yasewera iyeyo wamenyanawo 10 okha enawo pa benchi koma yachinyako CHIGOLI CHIMODZI ndi Assist imodzi, koma PANO akuyimba Njonjonjo ku Mpira kuli Chimwemwe 🔊🔊
Mukuona kuti wapezekako bwanji Katswiriyu?
Follow Mtonda Land Consultancy
03/06/2026
Layiniapu ya Ma player omwe Kalisto Pasuwa wawasiya koma amayenera kuwatenga ku Flames squad yokakumana ndi Ethiopia mu masewera opimana mphavu Ili CHONCHI komaso apa Benchi 👇
Uchizi Vunga, Dalitso Nahipa, Innocent Nyasulu, Charles Nkhoma
Maganizo anu ndiotani ngati akatswiri otsata Mpira wamiyendo ku Malawi?
Follow Mtonda Land Consultancy