31/03/2022
Vincent nyangulu
the
this page is for wanderes only, aim is update every news for our team
31/03/2022
Vincent nyangulu
the
31/03/2022
Vincent Nyangulu wasainira contract ya dzaka ziwiri ndi team yake ya Mighty wanderers
31/03/2022
BREAKING NEWS
Osewera wa Mighty Wanderers Vincent Nyangulu sopano watikitira comtract ndi timuyi, Masiku apita wa zinamvekapo kuti Nyangulu akulowera ku Nyasa Big Bullets koma lero Zatsimilizika kuti katswiri yu akhalabe ku Wanderers mpaka 2024
Sports Torch
Sunday pa Chiwembe tikumana ndi Tigers
Today 6 July Noma Vs Bullets @ Kamudzu Stadium
Peter Cholopi Ndi Lucky Malata Wawo Wapsa Waku South Africa
Malata Komanso Cholopi Anyamuka Lero Kukayesa Mwayi Ku S A Ku Team Ya Free State Stars.
Tafunire Zabwino Zonse Anyamata Athuwa Kuti Zikayendere Bwino.
This Weekend Noma Vs Civo @ Civo Stadium
manoma woyeeeeee!!!
Welcome To New Wanderes Football Club Page, Chonde Tiziziwitsana Zoona Zokha Zokha Za Team Yathu Yokondedwayi