Our home,our pride,our team
Namias United FC
its all about namias united fc,how it started and whats so special about the team
We are here
Good morning United fans
Weekend yanu ikuyenda bwanji
*NAMIAS UNITED FOOTBALL CLUB*
Pomwe tinali pa chisangalaro cha Eid week yatha,ma program anthu okhudza recruitment ya anyamata a U-19 siinayende mmene timaganizira.
Kotero training komanso kupeza anyamataku kuyamba Lachiwiri pa bwalo la Namias.Chonde tiyeni tibwere mwa unyinji.
Tiyeni tiwaziwitse azanthu mmadera osiyana siyana.
*Madzi komanso nthochi za ulere mma siku onse ama trial's*
*Note*
Osaiwala kutenga zosewerera mpira.
MANAGEMENT
08/04/2024
EKHAYA LUXURY RESORT LEAGUE is back,as defending champions,we started the league with a win.Remember that we are the Namias United.Kutchaya Kugwetsa
Moni kuchokera Ku team yanu yokondedwa ija (NAMIAS UNITED FC).
Tikupepesa kamba kosakupatsirani ma updates ama games osiyanasiyana omwe amamenyedwa nkati Kati mwa chakachi,izi ndikamba kq vuto la makina athu,koma pano zonse zili bwino,tikhala tikukupatsirani kalikonse.
In united,we all trust
(Lake side giants)
*MANGOCHI YOUTH FOOTBALL COMMITTEE*
KATSWIRI FIRST CAPITAL BANK U 19 LEAGUE
*MATCH DAY LIVE*
_NAMIAS UNITED FC_ 5️⃣-1️⃣ _NGOYI STARS FC_
Lester ⚽⚽
Rafick⚽⚽
Junior⚽
Full-Time
*MANGOCHI YOUTH FOOTBALL COMMITTEE*
KATSWIRI FIRST CAPITAL BANK U 19 LEAGUE
MATCH DAY LIVE
_NAMIAS UNITED_ 3️⃣-0️⃣ _LILANGUKA_
Lester⚽⚽
Leni⚽
FULL-TIME
02/09/2023
Player of the month, receiving 2KG maq soap
02/09/2023
Man of the match receiving K2000
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Contact the business
Telephone
Address
Mangochi, Monkeybay Road, Just After Ekhaya Resort
Mangochi