Matthew's moyo

Matthew's moyo

Share

Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Matthew's moyo, Sports Promoter, Mzuzu.

17/01/2025

Abale Lay B Salima wayamba kuimba zichani izi?

Atafunsidwa wayankha kuti khumbo lake ndiloti abooleze Music industry ya ku Tanzania

Mwana uja wayamba kuimba chiswahiri zitithandiza izi? His now song called "BLAFU" Now Out

17/01/2025

Mellz Kumpanje 💪💥

Chomwe ndimaziwa ine ndi chakuti "Munthu sumacheza wekha"...akulu akulu, uyu ndili naye pa chithunziyu ndi Bandera music ...ndipo ndikukhulupilira kuti tonse Pano nkhani yake tikuidziwa...ndikunena Pano,adakali mmanja mwa a police akumusunga mchitokosi...fast fast forward, munthuyi akukanika kutuluka kunali kuja chifukwa alibe lawyer omuthandizila kuti nkhani ikambidwe imalizidwe kuti atulukeko...nde ine ndili ndi mzanga lawyer amenenso ndi DJ, ndayesa kukamba naye... kutengera ndi mmene ama chargila ma lawyer komanso poti ndiwaku Blantyre,Kwa ineyo ndikuona kuti ndi fair price kutengela ndi mtengowo, koma mwandekha ngati munthu sindingakwanise...wanena kuti timupase MK650,000 mmalo mwa 1,000,000 pakuti Bandera ndi munthu oti tonse Tili mu field imodzi...koma pamwamba pa 650 timuikilepo MK500,000 yamafuta yoyendera 3 hearings...imene tikawerengera ikukwana MK1,150,000....nde ndimati ndikupempheni mundithandize limodzi limodzi kuti ndalamayi ikwane timutuluseko m'bale wathu uja ngati kuthekela kutelo muli nako...any amount will appreciated....Ayao amzanga tiliko Mesa??....

You can send through these accounts :

Airtel money : 0995072049 (Mellanie Joseph Msumba
Mpamba : 0885531911 (Kevin Chidothi)
National Bank : 1008151818

Ma transaction onse ndizaika pa page p***a muzaone...

Zikomo Mulungu akudalitseni🙏

14/01/2025

Morale the trapper mkana ntchulako ma artist angapo omwe akafuna kupakula and opakula wo ose mkanawa ntchula
Ife 500 pin tika wina ku bet tikukholan 🤣🤣🤣

12/01/2025

The Martse Foundation has announced that the Martse Memorial Show will happen on 24th May, 2025

Photos from Matthew's moyo's post 06/08/2024

Eeish Afana Ceez 🔥💯🔥

Anthu ochuluka atutumuka ndi oyimba Afana Ceez yemwe wapanga zinthu zachilendo pojambula nyimbo yake yotchedwa PAKALA PAKALA galimoto lomwe amagwiritsa ntchito ya Gusheshe itanyamulidwa ndi Crane m'malere, ndipo ena akuti izizi zikutanthauza kuti music industry ikusintha ndipo oyimba ayamba kupanga zinthu zawo mwadongosolo, onerani nyimboyi pa link ili mmusiyi

https://youtu.be/uLBiaa5NdC8

28/07/2024

A Jolasto inuo mukusowatu bwa?

Photos from Matthew's moyo's post 24/07/2024

Jay Jay Cee Mw ft ELI Njuchi awo
Driemo handede
MZUZU MAFIA ft Nepman
Link in comments section 👇

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Mzuzu?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Telephone

Address


Mzuzu