10/05/2025
Zikuchitika 0-1
WELCOME to the official page of IGWE STARS FOOTBALL CLUB
10/05/2025
Zikuchitika 0-1
Walelo
Igwe stars vs bawula united
3:00pm
29/11/2024
MA IGWEEE STARS
Tiyeni tipeleke dhola mwa unyinji nthawi yatha, trip yomwe tinkafuna ndiyomweyi,
NB; kulibe kutolera ndalama galimoto itafika kale waliyose wamanye ichoo yewo.
π€π€β½
25/11/2024
NEXT MATCH
IGWE STARS VS MKONDEZI FC
1 DECEMBER, SUNDAY
MKONDEZI GROUND
β²οΈ: 2:30 pm
β½π€π€π
K3000
Tiyeni tikayipatse moto, uku ng'oma zikalireπ₯π₯π₯
Haye haye ma igwee
Tisunge Chuma next week tiyendeko takhalitsa
Official update tibwera nayo mawa mungokhala okonzeka
β½β½β½
03/11/2024
Inkosi Lestar Ndine celebrates his birthday today.
HAPPY BIRTHDAY champβ½. Enjoy your dayπ€π€π
NB: MA dance yaliko tisangane ku Club Houseπ
πβ½
Eyo!! Igwe stars are you ready ? Next game tipite kutiko? perekani maganizo tikafika komwe mukufunako
igwe amakana zowalirana
β½β½
07/10/2024
MA IGWEEE STARS
Kulephera kwa game ya last weekend tonse zinatisokoneza koma tiziyiwale kuti tione chitsogolo basi,,
Nkhani yoti tikambilane lero ndiyoti tinve maganizo awina aliyese kuti tipange chinthu chimodzi, nkhan ndiyoti ma guyz aku mkondezi Kuja akuti tingavaye this week?
Nde decision tipange limodzi kuti zitha kutheka kupita week ino or next week,
Tiyeni nayoni ma igweees
π€π€π
HAYE HAYE ma igweee stars
Saturday tikukayakitsa motoo pa Maganga ground π₯π₯π₯
Tiyeni tisonkhe mwa unyinji tikayipatse support team bakamanye kuti isee saza tilije β½β½β½π
It's a IGWE STARS VS MASASA FC
π€π€ π
20/09/2024
OUR NEXT MATCH
FRIENDLY
β½ IGWE STARS VS BAULA UNITED
π Sunday, 22 September 2024
ποΈ BAULA GROUND
β 2:30PM
We are igwee stars πβ½π€π€
π₯π₯π₯π₯π₯π₯
Osasonkha sapita nawo!!!β½tiyen! tiyen!!
On sunday 22th september ku mzimba
Bawula united vs igwe stars
Wene mzimba mafumu pa zgaro yakwiza β½β½β½π