Zathuzathu Sports Page

Zathuzathu Sports Page

Share

Sangalalani Ndi Zamasewero Zotyakuka Ndi Zathuzathu Sports Page

Photos from Zathuzathu Sports Page's post 31/08/2026

Confederation of African Football (CAF), yasankha oyimbira asanu kuti akayimbire masewero a mpikisano wa Champions League komanso Confederations Cup.

Easter Zimba ndi amene adzaimbire masewero a Confederation Cup pakati pa Unam FC ya ku Namibia ndi Kabuscorp de Palanca ya m'dziko la Angola pa bwalo la Luanda Estadio 11 de Novembro pa 5 September 2026.

Samuel Fudzulani ndi Lameck Phiri asankhidwa kuti akagwire ntchito ngati othandizira pamene David Chinoko ndi amene akakhale oyimbira wapadera.

Chinoko wapatsidwanso masewero a Champions League pakati pa Foresters FC ya ku Seychelles ndi Willete de Benguela omwe adzaseweredwe pa 10 September 2026 pa bwalo la Lubango-Estadio Nacional da Tundavala.

Fudzulani komanso Sibusiso Sibande ndi amene adzagwire ntchito ngati othandizira patsikuli, pamene Zimba ndiamene adzakhale bwana wa oyimbirawa.

Mkulu wa oyimbira ku Football Association of Malawi (FAM), Duncan Lengani, wati ndiokondwa ndi chiwerengerochi zomwe zikuonetsa mpira ukupita patsogolo.

31/08/2026

The five highest-paid footballers on the African continent are all playing in Libya.

1. Fiston Mayele ๐Ÿ‡จ๐Ÿ‡ฉ | $5 million | Al Ahli Tripoli

2. Kwasi Sibo ๐Ÿ‡ฌ๐Ÿ‡ญ | $5 million | Al-Swehly

3. Mohamed Tougai ๐Ÿ‡ฉ๐Ÿ‡ฟ | $3.7 million | Al Ahli Tripoli

4. Jean Claude Girumugisha ๐Ÿ‡ง๐Ÿ‡ฎ | $2.4 million | Al Ahli Tripoli

5. Lameck Banda ๐Ÿ‡ฟ๐Ÿ‡ฒ | $1.85 million | Al-Swehly

31/08/2026

Bungwe la FAM lalengeza kuti masewero a ndime yotsiriza ya chikho cha Airtel Top 8, pakati pa Mighty Wanderers ndi Ekhaya FC, atulutsa ndalama zokwana K87.3 million.

Masewerowa anachitikira pa Bingu National Stadium ku Lilongwe la mulungu, pa 30 August, ndipo Ekhaya FC inagonjetsa Wanderers 2-1 kuti ikhale katswiri watsopano wa chikhochi.

Mkulu owona za malonda ku bungwe la FAM, Mayamiko Kafwamba, watiuza kuti, pa ndalamazi, ma timu a Wanderers ndi Ekhaya atenga K12.6 million timu iliyonse.

Malinga ndi a Kafwamba, ndondomeko yogulitsa ma tikiti pa tsiku la mpira lomwelo inathandiza chifukwa kunalibe ma tikiti a chinyengo.

Koma a Kafwamba ati mchitidwe wa anthu ena ochepa, olowa m'bwaloli modumpha mpanda kapenanso kubowola wire, amene anazungulira bwaloli, unachitika.

Iwo ati bungwe la FAM lipitiriza kukambirana ndi nthambi zokhudzidwa, kuphatikizapo a chitetezo, pofuna njira zothetseratu vutoli pamene timu ya Flames idzikonzekera kusewera ndi South Sudan mu Africa Cup of Nations mwezi wa September.

31/08/2026

FAM YASANKHA BOB MPINGAJIRA KUKHALA MPHUZITSI WA FLAMES U-23

Pasanathe maola 24 timu ya Mighty Wanderers FC itaimitsa ntchito a Bob Mpinganjira, bungwe la Football Association of Malawi (FAM) lamusankha kukhala mphunzitsi watimu ya dziko lino ya osewera osapitilira zaka 23.

Pakadali pano, timuyi ikuyembekezeka kukumana ndi Eswatini mu gawo loyamba la masewero ozipezera malo ku mpikisano wa U-23 Africa Cup of Nations.

Masewerowa akuyembekezeka kuchitika pa 28 September 2026.

31/08/2026

Mighty Wanderers FC have suspended head coach Bob Mpinganjira with immediate effect following a string of inconsistent performances, including their defeat to Ekhaya FC in the Airtel Top 8 final.

The Nomads announced the decision in a statement signed by Board Secretary Chancy Gondwe on behalf of the Board of Directors, without giving specific reasons for the suspension.

The club said it will appoint an interim head coach within the next 48 hours as it moves to restructure the technical panel.

30/08/2026

Timu ya Ekhaya ndi akatswiri achikho cha Airtel Top 8 Zamadolo atagonjetsa timu ya Mighty Wanderers 2-1 bwalo la Bingu Ku Lilongwe.

Ekhaya inapeza zigoli zake kudzera kwa Blessings Malinda komanso Allen Chihana pomwe Wanderers inagoletsa kudzera mwa Mphatso Kamanga.

Timu ya Ekhaya yatenga ukatswiriwu pamene kanali koyamba kusewera nawo mu mpikisano wa Airtel Top 8 Zamadolo.

25/08/2026

Msika wogula ndi kugulitsa osewera watsegulidwa lero.

Bungwe loyendetsa masewero a mpira wamiyendo la Fam lalengeza izi kudzera patsamba la mchezo.

Malinga ndi bungweli msikawu udzatsekedwa pa 21 September.

Izi zikutanthauza kuti matimu ali ndi ufulu wogula kapena kugulitsa osewera pakadali pano.

Pakadali pano katswiri wa Blue Eagles Fahad Mcheka komanso Rashid Dah wa Luanar Mitundu ndi ena mwa osewera omwe akufunidwa kwambiri.

25/08/2026

FCB Nyasa Big Bullets have signed a 26-year-old Liberian, Sheku Sheriff, from LPRC Oilers on a two-year deal

Maule mwamulandira bwanji katundu ?

22/08/2026

Today's results

21/08/2026

๐Ÿšจ ๐Ž๐…๐…๐ˆ๐‚๐ˆ๐€๐‹: Premier League has confirmed ๐ง๐ž๐ฐ ๐ซ๐ฎ๐ฅ๐ž๐ฌ for the 2026/27 season. ๐Ÿ“‹๐Ÿด๓ ง๓ ข๓ ฅ๓ ฎ๓ ง๓ ฟ

โœ… ๐๐ž๐ฐ ๐ซ๐ฎ๐ฅ๐ž๐ฌ ๐›๐ž๐ข๐ง๐  ๐ข๐ง๐ญ๐ซ๐จ๐๐ฎ๐œ๐ž๐:

โฆฟ Injured players must now stay off the pitch for at least ๐Ÿ ๐ฆ๐ข๐ง๐ฎ๐ญ๐ž, up from 30 seconds

โฆฟ A ๐Ÿ“-๐ฌ๐ž๐œ๐จ๐ง๐ ๐œ๐จ๐ฎ๐ง๐ญ๐๐จ๐ฐ๐ง for throw-ins and goal-kicks, with the restart reversed if delayed

โฆฟ Substituted players have just ๐Ÿ๐ŸŽ ๐ฌ๐ž๐œ๐จ๐ง๐๐ฌ to leave the field, or their replacement waits until the next stoppage

โฆฟ A new VAR review specifically for clearly ๐ฐ๐ซ๐จ๐ง๐  ๐ฌ๐ž๐œ๐จ๐ง๐ ๐ฒ๐ž๐ฅ๐ฅ๐จ๐ฐ cards resulting in a red

โฆฟ A trial requiring managers to nominate an outfield player to leave the pitch for a minute whenever play is stopped for a goalkeeper injury

โŒ Whatโ€™s ๐ง๐จ๐ญ ๐œ๐จ๐ฆ๐ข๐ง๐  from this summerโ€™s World Cup:

โฆฟ Hydration breaks

โฆฟ VAR reviews for incorrectly awarded corners

โฆฟ The red-card protocol for players covering their mouths

โฆฟ Yellow cards being reversed for mistaken identity or diving, VAR can only correct who was booked, not the decision itself

๐ƒ๐Ž ๐˜๐Ž๐” ๐€๐†๐‘๐„๐„ ๐–๐ˆ๐“๐‡ ๐“๐‡๐„ ๐‚๐‡๐€๐๐†๐„๐’?

Want your business to be the top-listed Gym/sports Facility in Pretoria?

Click here to claim your Sponsored Listing.

Location

Category

Telephone

Address


Pretoria