30/08/2026
Martinez wayamba game ya Chelsea atangolengezedwa lero lomwelino kt ndi osewela wa Chelsea nthawi you mweyo wapezeka mu first 11 ya Chelsea kuluza ndekuti chikhala chitoso kuwina ndekuti akhala akutamidwa
Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Za masewelo Mchichewa, Sports, mondiwadalitso@gmail. com, Blantyre.
30/08/2026
Martinez wayamba game ya Chelsea atangolengezedwa lero lomwelino kt ndi osewela wa Chelsea nthawi you mweyo wapezeka mu first 11 ya Chelsea kuluza ndekuti chikhala chitoso kuwina ndekuti akhala akutamidwa
13/08/2026
Cameroon inakanika kuzigulila mmalo kuchokera mu group stage yomwe munali ma team 12 kuphatikiza Malawi chifukwa choti CAF imafuna kukhale ma team 16 anasankha ma team atatu chifukwa cha FIFA ranking omwe ndi Ivory coast, Egypt and Cameroon yomwe yafika finals
pangan follow page ino Za masewelo Mchichewa
mavuto a scorchers
1.kuchinyisa koyambilira tikukanika kupanga control pressure first 10 minutes
2.ma Arial balls (wa mmwamba) ma defender ukumawavuta kudula Game ya Egypt anachinya cha Head ya Ghana cha offside chija chinalinso chosumbilamo
3.kugwilisa ntchito ma Set peaces like ma Kona kick kukutivutabe Kusogolo kuja kuli madolo oti kumawapasa mipila yabwino azingosumbilamo
4.pena ngakhale ndi vuto losaonekela kwambiri tikumazasiilana kumaka kujejemesana tokhatokha
5. Goalkeepers trainer Ali ndi ntchito ngakhale last game zinali bwino koma sizoti tikukhulupililapo bwinobwino pa Golopo koma pot ndi mpira tiwalimbikise zabwino nde ndi zambili kuposa mavuto ochepa tatchulawa
pangan follow page ino kt zisamakuphonyen@
10/08/2026
Mulungu anatibisila mmawa osamatha mawu
pangan follow page ino Za masewelo Mchichewa
Fazili sakumaima pa touch line chifukwa alibe license osati ndi kunyada tikunvana kumeneko
pangan follow page ino
10/08/2026
Mulungu anatibisila mmawa muli naye mangawanso ngt ?
follow this page
Game yatha koma ngt tisagone eti?😂😂
09/08/2026
chipogwetu akuti yachitipayo ndi Honda freed
08/08/2026
silver yasegula gap ya 2 points pamwamba pa wanderers yomwe yaphovomoka pa top atakhalapo kwa masabata awiri
pangan follow page ino Za masewelo Mchichewa
wanderers yataya 3 points yokomola kale mmalo mophelatu moyale inasisimuka mpaka kubweza chigoli cha kumapetopeto kt ithele 1-1