Mpira watha Mighty Wanderers yafika mundime ya quarter finals ya chikho cha FDHBANK lero itakwanitsa kugonjetsa team ya Mzuzu City Hammers pa bwalo la Rumphi ndipo zigoli zinchoka Kwa Blessings Singini mchigawo choyamba pa mphindi 33 ndipo chachiwiri anagoletsa ndi Muhammad Sulumba pa mphindi 49.Apa tingoti Ambuye zikomo.
Game yotsatila ndi Tnm superleague pa 14 September 2025 ndipo tili koyenda kusewera ndi Silver strikes pa bwalo la silver ku Lilongwe.
Chaka Cha Mayakho ku Manoma
Sports
90+3 added
Still
Mzuzu 1-2 Noma
87' gone
Still
Mzuzu 1-2 Noma
75'
Kaliati and sulumba out
Kamwendo and Manda in
Still
Mzuzu 1-2 Noma
70' gone
Mzuzu 1-2 Noma
68'
Mzuzu 0-2 Noma
Singini and sulumba
60 '
Kudonto out
Cholopi in
Still
Mzuzu 0-2 Noma
56' gone
Still
Mzuzu 0-2 Noma
Sulumbaaaaaaaa
Goalooooooo
Mzuzu 0-2 Noma
47'
Chigawo chachiwiri komanso chomaliza chayambika tsopano
Mzuzu 0-1 Noma
46'
11/09/2025
Tipumile tsopano
45+5 added
Kuti ma team akapumile momujabe
Mzuzu 0-1 Noma
34' singini
Click here to claim your Sponsored Listing.
Location
Category
Contact the business
Telephone
Website
Address
Lalilubani
Blantyre