16/05/2026
Week 3 as it stands π₯
Football is a therapy...
16/05/2026
Week 3 as it stands π₯
16/05/2026
FDH Bank Premiership
-Creck Sporting 1-3 Kamuzu Barracks
-Chitipa United 1-0 Civil Service United
-Luannar Mitundu FC 0-2 Mighty Wanderers
-Ekhaya FC 2-0 Moyale FC
Super League of Malawi (Sulom) yatulutsa ndondomeko ya masewero a season ya 2026/2027 kuyambira loweruka pa 25 April, 2026 mpaka pa 20 February, 2027.
Tsiku lotsegulira, akatswiri Mighty Wanderers adzayambira ndi masewero apa khomo pa Kamuzu mu nzinda wa Blantyre ndi Karonga United, pamene FCB Nyasa Big Bullets iyamba ndikoyenda pamene idzasewera ndi
Civil Service United pa bwalo la Civo ku Lilongwe, ndipo
Kamuzu Barracks idzaitanitsa Silver Strikers pa bwalo la Champions ku Dowa, pamene Moyale Barracks idzaswana ndi Goshen City Dedza Dynamos pa pa bwalo la Mzuzu.
Ndipo pa tsiku lotsatira, lamulungu pa 26 April 2026 timu ya Blue Eagles FC idzakumana ndi Ekhaya FC pa bwalo la Nankhaka mu nzinda wa Lilongwe, pamene Red Lions idzakumana ndi Creck Sporting Club pa bwalo la Balaka, ndipo Mafco FC idzathana ndi timu ya Mitundu Baptist pa bwalo la Champions ku Dowa, pamene Masters Security FC idzaitanitsa Chitipa United pa bwalo la Civo mu nzinda wa Lilongwe.
Mlembi wa Sulom yemwenso ndi mkulu wa komiti yoona ndondomekoyi, Williams Banda, wauza atolankhani lero mu nzinda wa Blantyre kuti ndondomekoyi yatulusidwa mogwirizana ndi kalendala ya Football Association of Malawi (FAM).
Banda wati salola kuti matimu azipempha masewero oyenera kukumana nawo kamba koti izi zimasokoneza.
Iye waonjezera kuti timu ina iliyonse ikuyembekezereka kusewera pafupi-fupi masewero asanu ndi awiri pa khomo, likamatha gawo loyamba ndipo ena adzasewera gawo lachiwiri.
# football season is back π₯π₯π₯
mongokumbutsana zinali lero ku area 30 pa Nnkhaka ground mu TNM Super League,
FCB Nyasa Big Bullets 0:0 BLUE Eagles FC, Ma Eagle...
Mighty Wanderers yagonjetsa Jwaneng Galaxy 1-0 pamasewero a mpikitsano wa CAF Confederation Cup omwe analipo lero pabwalo la Bingu mu nzinda wa Lilongwe.
Felix Zulu anagolesera Manoma mumphindi 80 kupangitsa kuti apeze chipambano pa masewerowa.
Masewero a chibwereza alipo kumathero a sabata ikudzayi m'dziko la Botswana.
80'
Felix Zulu scores
Mighty Wanderers 1-0 Jwaneng Galaxy
#
π Elgeco Vs Silver
54'! goaallπ₯ Andrew Joseph equalises for the Bankers.
Elgeco 1-1 Silver Strikers
21/09/2025
Koma ase Jwaneng Galaxy FC chikukulimbitsa mtima ndi chiyani koma? Lero uyidziwa Bangwe. π
Unofficially Rerenye zikupweteka.
predict the final scores and stand a chance of winning k2000 airtime.
zoyenera kuchita.
β’like this post.
β’share this post
β’like and follow this page..
uwu ndi wamotoπ₯π₯π₯π₯
20/08/2025
π¦π¨ππ¨π ππ ππππ ππ§ πͺππ‘πππ₯ππ₯π¦ ππ¦ ππ’π π§π’π¨π§π¦ πππ¦ ππ‘π§ππ₯π‘ππ§ππ’π‘ππ ππ«π£π’π¦π¨π₯π
Veteran Striker, Muhammad Sulumba has penned a seven-month deal at Mighty Wanderers FC with Coach Bob Mpinganjira describing his arrival at Lali Lubani Road as a major boost to the CAF and Super League campaigns.
Speaking after putting pen to paper, Sulumba said he is happy to be back at Wanderers and he hopes to contribute his talent and experience to propel the Nomads to desired levels.
Head Coach Bob Mpinganjira has since hailed Sulumba's signing as a good add to his squad ahead of CAF Confederation Cup assignments and league campaign. Mpinganjira hopes the arrival of Sulumba will add experience to his attacking line as he seeks to address scoring woes.
Sulumba who last featured for Wanderers in 2023 arrived in the country early this month after a stint in Libya. Apart from playing for Wanderers, Sulumba also featured for FCB Nyasa Big Bullets, Civil Service United and Creck Sporting among others.
17/08/2025
ayi zikomo,ππππ