01/09/2026
MUST Dragons & Phoenixes lero kuli birthday ya captain wawo🎂🎂...Inde mwawerenga bwino ndithu kuti ndi birthday ya a Manzy😅
Ife kuno tingoti Hapoy birthday Captain🎂🥳
Zimene mupange comment pa post yi, ngati zili zosemphana ndi birthday, ife ma Trojans sizatikhudze😂😅
Volleyball Yathu Volleyball Malawi
30/08/2026
Patali utha kumaona ngati ndi team ya Volleyball koma ayi ndithu Masintha Choir yeni yeni😂
Titha kutsimikiza kuti Makosana wa luso alibe kaye pakadali pano😂
MUBAS TRUPACES muchititsa manyazi ma Public Universities why?💔💀
29/08/2026
Kodi iwe admin wa MUBAS TRUPACES magame sanathebe mpaka pano?(19:09)😂 Upangatu zofoira iweyo😂😂
24/08/2026
🚨WEEKEND VOLLEYBALL FRIENDLY GAMES
Amuyedzeka osati zibwana😂
MYUBAS TRUPACES 1 - 3 Michonya
MYUBAS TRUPACES 1 - 3 Thunders
Admin wa MUBAS TRUPACES ati ali busy kaye😂💔
22/08/2026
Good Morning!
ku BICC ma drone agwira ntchito ya bho heavy😂🔥
12/08/2026
Call us "Chawinga Trojans Volleyball Team" please 😊😂
07/08/2026
Happy 18th birthday Lusungu🥳🥳
Kukhala beautiful komaso dolo sizinthu zophweka🔥🔥
Enjoy your day😊
02/08/2026
Enjoy the Holiday and train harder! Avoid tima miniskirt makosana😌😂
24/07/2026
Ma Trojans mwadekhatu😂
Mayeso akubwera bwa? Tidusa koma?😂
13/07/2026
All the Best ma Trojans🔥💪